Email a copy of 'Judge postpones Malawi 'Cashgate' convict sentencing' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Judge postpones Malawi 'Cashgate' convict sentencing' to a friend
The ruling Democratic Progressive Party (DPP) has been accused by Malawi Parliament’s Budget and Finance Committee of fuelling the plundering...
This is obscene bwanji. Look at that house! Ndalama zokubazo kutasa nazo choncho?
The defence lawyer’s argument is dangerous and counterproductive. This woman deserves life sentence because she is a murderer. How many people lost their lives because of her acts in hospitals. Surely common sense tells me that some part of the money she stole was meant to buy medicine for Malawi hospitals. At the time she stole our money, there were reports that people were dying in hispitals because of lack of medicine. Apite kundende. Nga macourt alephera our ancestral spirits will commit her to death sentence.
Imeneyi nyumba yamunthu wogwira ntchito m’boma? Koma ngati mumayankhula n’Chauta, ayi tiuzeni verse yake nafe tiyeseko!
@ 48, Mwapheranjiru is right!!!! Eeeehh!!!! Imeneyi nyumba ya munthu wogwira ntchito kapena wa bizinezi? Even Mulli Brothers MD, Leston, nyumba ngati imeneyi alibe!! Fufuzani pena pali pose. Zonse walembazo inenso ndikugwirizana nawe! First step should be kumulanda Chuma chonsecho, then sending her to jail! But to be frank with you my fellow readers, I have doubts with the credibility of this Judge. I would be comfortable if it was Chifundo Kachale, Dustain Mwaungulu, Anaclet Chipeta and/or Edward Twea.
have your say malawians
A Malawi, imeneyi nyumba ya munthu wogwira ntchito mu boma? Bvuto ku Malawi liripo chifukwa boma likulekerera anthu kumaba. Munthu wolandila K150 000 pa mwezi akupedzeka ndi ulemerero wa ma billions, koma boma kumangoyang;ana. Mai uyu afufudzidwe ulemerero wache wonse umene ali nawo moyenera ndi ndalama zimene amalandira pa mwezi. Zonse a boma landani, zonsezo ndizakuba. Palinso anthu ambiri mu boma ali ndi ma nyumba mu Lilongwe oposa iyi mwainjambulayi, koma boma lingowayang’ana. Mboni, mboni ya boma chani, samalirani. Mai uyu alandidwe manyumba onse amene wamanga. Komanso boma lifufudze kumene ena anapedza ndalama zomangira manyumba tate house ao. Ena amanama… Read more »
EQUATE THIS OPULENT MANSION TO LIVES LOST, ROTTEN DEAD BODIES IN MORTUARIES, HER AFFLUENT LIFE STYLES, HER FROM RUGS TO RICHES STORY, HER CHILDREN EDUCATION FROM THE LOOT AND THE STATEMENT FROM HER LAWYER LECTURER. DO YOU GET A DIVIDING LINE IN REASONING CAPACITY. THE BEST JUDGE FOR SUCH CASES ARE DUNSTAN MWAUNGULU OR ANCLET CHIPETA WHOSE POCKETS HAVE NOT BEEN TAINTED OR WHOSE JUDICIAL BRAINS HAVE NOT BEEN CORRUPTED. I SAID IT THE OTHER TIME ON THIS VERY PAGE KUTI WE HAVE VERY FEW LECTURERS AT OUR UNIVERSITIES WHO HAVE HOLISTIC INTELLECT STILL INTACT IF WE WERE TO GO… Read more »
Ngati munthu wa bweza musiyeni limbanani ndi enawo
Have your time mr judge for people are watching.wishing you a 9c judgement
It’s very painful. Paying taxes for other people to enjoy. Look at her mansion and look at her salary. Its better you stop us paying taxes. Shiiitiii. bloodful zanu asokonombwe, achamumatowo, amununkhadala, mbozi, agalangánda, agulukunyina,