Email a copy of 'Kabwila brands Mutharika ‘inept': Insists Malawi President should ‘humbly resign’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

84 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
peter
peter
8 years ago

indeed wwhen someone is failing to take care of the nation, its better to advise him before he conjure into this senario of rsignaton

flying- eagle
flying- eagle
8 years ago

Kodi ndi ndani angalamulire malawi anthu nkusangalala? Sikuti APM sakulakwisa ayi, zilipo zambiri koma vuto tilindi poor politicians. Can one define politics cleary? Ngati vuto la chakudya kodi tikudziwa source yake? If yes, Nanga tuchitapo chani? Kodi atsogoleri ena sanayambitsepo programmes othandiza a malawi? Inu amulowa mmalo ma programmes wo simukuwaphatikiza ndi ndale? Vuto la food shortage, kodi green belt initiative singakwanitse kulichepetsa ngati boma litaikapo maso ake onse ngati umo achitira pa nkhani za treason? Tisiye kulozana chala inutu simukumva njala tikumva ndife, ndu nenamu ndulephera kumalizitsa ma phunziro anga a public administration chifukwa cha fees koma simungandithandize student… Read more »

mayo mayo
mayo mayo
8 years ago

Zoona Mayi

mayo mayo
mayo mayo
8 years ago

Kabwila mulekeni peter alamule akazafuna azasiya yekha mpando szimenzo zompanganazo sibho iyetu analipeza boma kulibeko kathu cashgate nde muthu akuyesesesa mbali yache leave him mukakhala nd phuma simuzawinatu ayi mulungu nd yemwe akuziwa azawekuza yekha remember kamuzu sadathamange sadafulumile das y lelo muli nd ufulu ugwilisen tchito ufuluo osat kumapangana zolanda boma ayi

c-b
c-b
8 years ago

kabwira plz usasokoneze anthu osabweretsa phoko kudziko lanthu la malawi,,,mukanakhala ofuna kuthandiza bwezi mukubwera poyera ndikumuwuza pter mutharika zoyenera kuchita kuti mavuto alipowa anthe komaso mwagawa chimanga chochuluka bwanji kwa anthu ovutika ndi njala ?nanga mukamati mukuva chisoni ndi anthu akuvutika ndi njala mukutathawuza chani ?mutharika ndi m’malawi ngati inu akabwira nose muli ndiundido othaza anthu akutikawa .!osamangoloza chala munthu kuti walephera musanamuthandize kuti akoze zinthu,,let me remind u ths anthu akunja akamawona amalawi akuvutika amati amalawi akanika kuthandizana osati mutharika yekha coz inu mukuyene kumuwuza muthalika zo chite koma mumangonyoza kodi kumeneku ndikuthandiza? ndikupheni a mcp makamaka iwe kabwira… Read more »

marika
marika
8 years ago

Peter sakulakwa chilichonse komaso mavote adawina. Kodi ulamulilo wa mmbuyomu anthu samagona ndi njala? Kodi apa pali chifukwa choti President atule pansi udindo? Inu chemwali PhD satengera ku Chancellor College. Bolani mukanatengera ku Harvad of Africa, South Africa. Dyera lofuna udindo apa likuoneka. Pepani cashgate kawiri ayi. tamakangophikani nsima ndi chibwaka. Amayi kuba bolankoniso Joyce Banda ali ndi nzeru. Inu mkamwa ndi kusuta chamba basi. Mulibe ma qualities a leadership koma violence ndi distruction. This is a peaceful nation, we don’t want your violent acts. Go to hero!!!!!!!!!!!!! Peter is still the leader and we are in support of him,… Read more »

YAKASHATA
YAKASHATA
8 years ago

Munthu akakhala hule samasowa, nthawi zambiri amakhala opanda ulemu Kabwila is showing all signs of a prostitute someone who is frustrated . You supporters of MCP, Do you expect respect for Chakwela from southerners when he gents into power ? Chapita nzako chapita mawa chiri kwa iwe. A MCP mwaiwala zomwe munkapanga mukulamulila. Mwaiwala njala ya 1981 ? UFITI ETI ? NJALA YENIYENI MUDZAKUMANA NAYO MTSOGOLO MUNO, MULUNGU SIWAMASEWELA

Commenter
Commenter
8 years ago

Bravo Jessie Kabwila, please tell him like it is. We do not recognize him as president of Malawi because he has failed on majority of his duties and our state. We as Malawians do not need to suffer at the hands of one greedy president while the rest die in hospitals and at their homes. We are not afraid of him, our country went into democracy and he should accept his failure, the same way we voted him into power is the same way he shall be booted out. We are not afraid of him, he is a mere human… Read more »

Winston Msowoya
Winston Msowoya
8 years ago

I overwhelmingly agree with Kabwila’s assertions that Muthalika must step down in the wake of his incompetence and tribalistic leadership.Malawians,we have suffered immensely under obnoxious leadership before,once beaten twice shy.We must not again give another chick.However,Muthalika and his corrupt late brother Thom,have not suffered in the struggle for the independence of our dear Malawi.These two brothers are impostors without vision and sense of patriotism.The gallant youths of Mzuzu,have shown the way therefore,Malawians of all walks of life must join this noble struggle to bring back our democracy and decorum.What Muthalika and his serviiles are doing today,is to destroy and impoverish… Read more »

box13 bilila NU
8 years ago

Hahahha kabwira ndi mphaka ndi nzake chakwera kip on drmn until jesus cmz.peter munthalika BOMA!!!!!!!!!!!!usamayesa zida magetsi atathima.Mapwiya umwewo mpaka 2024 BOMA!!!!!!!wina ufuneusFune.

Read previous post:
US, Malawi sign military agreement        

Malawi and United States have agreed to a major military cooperation which Minister of Foreign Affairs and International Cooperation George...

Close