Email a copy of 'Kabwila donates towards maternal health in Salima: K1.5m worth bicycle ambulances' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Kabwila donates towards maternal health in Salima: K1.5m worth bicycle ambulances' to a friend
In a quest to popularize the 90-90-90 targets enshrined in the 2015-2020 National Strategic Plan (NSP), the National Aids Commission...
Useless illmind for #11,16,20. Kuganiza mopusa
Zingaoneke ngati wapangazo ndizopanda pake kwa ena ,koma kwa ife tili kumudzi tikuti zikomo kwambiri ,pakati pausiku matenda akatibwelela timavutika kuyimba phone kuchipatala amatiyakha kuti fuel watha ayi yachokapo dikilani mawa mawa!!!ndiye ife tikuti zikomo ambuye akudalitseni Mai
Big up madam
Bolako
Great contribution madam MP. However, this should come together with awareness on family planning to encourage them use family planning methods.
Forsake,,,,,makani aja timaona ngati ndinu anzeru kuposa Kaliati,,,,koma ai ndithu bola kaliati ku mj west kwatukuka osati ndi nyasi zanu mukukamba apazi bicycle ambulance,,,,,,?wat 4,,,,,kwa kweni,,,,,,zikatere,,,,tikumakwera real ambulances,,,,,osatipusisa,,,kagwere naoni uko maphapha anu,,,,muzikanyamulirapo fodya,,,,,ndimziwira mai oyembekezera,,,,,mumnyamule panjinga can’t she deliver on her way?,,,,,,,,lol
Uyu ndiye munthu osati zinazi
I salute u Hon Jessie ma MP a
kwathuku ku mpoio sangachite
koma kumwa mkoniho basi.
Welldone kabwila,MP azitero
That is our expectation from you honourable mp we are proud of you and continue showing your action than words to give hope for malawians to vote for you come 2019.
Ambulances meaning trailers mounted on the bicycles? Is the local company that manufactured these trailers certified to make them? Are the trailers certified to carry patients? I think this is a risk to patients. Bwino muzamaliza miyoyo ya ma patient ndi mphatso zanu zopanda tanthauzozi.People must never be brain washed by these type of gifts. I would be cautious to allow my relatives to use this crap. If Kabwira is serious, then she should buy motor ambulances propelled by batteries considering the lack of fuel. They should be propelled like golf carts.