Email a copy of 'Kabwila explains ‘stealing from corpses’ comments amidst backlash' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Kabwila explains ‘stealing from corpses’ comments amidst backlash' to a friend
The Football Association of Malawi (FAM) Sunday awarded certificates on Preparatory Football Coaching to 21 football coaches drawn from across...
chitsiru cha munthu chimenechi, kuyakhula ngati akubiba. Ngati kuti alibe abale akachirombo. uzafa imfa yowawa Jessie Chindere kabwila. Paujeni pa mako
chitsiru cha munthu chimenechi, kuyakhula ngati akubiba. Ngati kuti alibe abale akachirombo. uzafa imfa yowawa Jessie Chindere Kabwila
Zachabe, zonse zili chabe…atelo mlaliki! we never knew that Kabwila’s mouth could voice such filthy comments, what do u pipo take Malawians for? usay one wrong thing today n tomorrow ucome and talk even more nonsense. watch ur toung madame spokesperson!
thats why banja linawavuta amayi wawa, if one can speak like that in opposition what if she in in government , that can be worse u have to apologise, dont you know that some of the members in in mcp are on ARVS/ TIMAWAONATU KU LIGHT SHAME ON YOU KABWILA
Malawians wake up chilungamo sichipheka and God is the righteous Judge.Courts are clossed but God’s eye is ever open to see us.Let God punish the one with evil motive in this issue.
Winawe ukuganiza ife a congrss we hate Jessy iiii not a single bit we love her just as we love our mighty party
Proud of our Jessy she has no match ndipo she will take soo head-on. Inu a HIV ndimabungwe any mukudana ndimunthu iyi skyline.yerani nkhondo ndinu prank inuuu mukusangalala ndikuberedwa??? Inu simukudziwa kuti anzanu sakupeza mankhwala mmidzimu ndiye first lady ideas zinyalala ndi alomwe kukatenga ndalama inu nkumalimbana ndi Dr Kabwila? Mwatani inu thinking yanu njotani yomvetsa chisoni chonchi??? Mayi wakustatehkuseyo apepese iyeyo palibe good judgement of all organizations why target NAC for contributions towards petty projects,?? Wish a Malawi!!!!
Special request to Jessie Kapasula Kabwila. It is not too late please apologize because if you DO NOT, this will haunt you and your party later.
Ine ulemu wanga pa inu ndichita withdraw.
I have all along respected Jessie but now I think I gave my respect to a wrong person. Jessie to regain my respect you need to withdraw the statement and apologize to us people living with HIV. Otherwise we will condemn you too.
The statement is not even ambiguous for one to be talking of semantics or misinterpretation ayi. If you are honest apologize please.
Takhumudwa nanu mayi
Pali anthu ena ouma mtima motelo kuti kuba alibenako chisoni kapena, manyazi angakhale nthumanzi, kotelo kuti akhoza kumubela m’mphawi mbale yokhayo alinayo. Panopa a Malawi tili pa umphawi wadzaoneni m,mbali zonse za Boma chifukwa cha cash-gate. Anthu ouma mtima chotele akhoza kubela maliro atapeza mpata. Ine ndikuganiza kuti izi ndi zomwe mai Kabwila amatanthauza osati kunyoza anthu a HIV/AIDS.