Email a copy of 'Kaliati slams DPP for beer subsidy to stop people from attending UTM rally' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

15 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
horrendous monster
5 years ago

Ku BT DPP inagula mowa.,..Ku LL DPP inapangitsa mpira…kuMuzu DPP….Kodi mmayesa mMoirawaku LLs unali was U20 under FIFA? Inuyo a UTM ndi a FIFA anayamba kupereka date lazochita anali ndani? Inutu zikuoneka kuti munasankha dala tsikuli kuti muzitibwatika kunamizira DPP. II’vetidzavotera mfundo osati kumveredwa chisoni chifukwa cha maboza mwamva ma crooks a UTM!!!. Kaya ndiye Ku Mzuzu DPP mwaipekerako zotani tidzaona.

mfundo apa
5 years ago

A ndele galimoto za mowa zinaima pati ndi pati? Iyitu ikhonza kukhala tactic yanu kuti anthu akumvereni chisoni. Nanga anaphunzitsa ndale kaliati ndindani? Mmayesa ndi Mulzi yemweyo. Izo nzachikale enafe pamtsokhano panupo timafunapo mfundo osati maboza. Utsogoleri wachoncho ndiuja anthu amadzalira nawo. Munditchulire malo omwe panaima galimoto zamowa osati maboza. Tikufuna mfundo APA Malawiaspite chitsogolo.

ndele
ndele
5 years ago

ndi cipani citi cisanatose ma rivals?????? ma plan ,zokamba zatha ncifukwa mmati aliyese aledzele kuzelezeketsa anthu nde makhala azibambo osamala mmakomo. zoona. koma yeah pipo of good will kuzelezeketsa anthu bwanji kungokhala pheee.
muluzi amanyoza a bwana malewezi kuti sangathe kulamula dziko amamwa zi ma tablets 50 pa tsiku, kodi ochoka nsana angalamule dziko? monga sacita manyazi lelo. anthu akuluakulu kunyonzana ,nanga lelo?????????????????????????????????
osaopsezana cooooonde. aliyese apange zinthu mwakufuna kwake. basi

amateur politics
5 years ago

Kaliati always full of accusing others mfundo njeee! Nanga jce and msce zatani? Kodi matchona akunenedwawo ndi ma graduates a unima anaonetsa luso lothekera kutukula Malawi ndi ndani? nanga nchifukwa çhani mumapititsa ana anu kukaphunzira kunja? Mukufuna muzitiputsisa kapena chain? kodi amangitsa maunirvesity okongolawo ndi ndani? Mmayetsa ndi matchona omwewo. Kaliati ndi UTM mutiuze mfundo osmangokhalira kupakana matope, ife ayi amateur politics. kaya kunali mowa we don’t care, koma tell us mudzatani osatinso mfundo ZANUzoberazo.

sinokha odzavota
5 years ago

A UTM mukufuna sympathy komatu anzanuwo angoti phe kumangokuwerengani. Nanga Kaliati ndi mama Kali cholombirana ndi prof getu nchani? Zikuonetseratu kuti kusagona tuloko nkhani ndï prof getu, akukuyabwani ndiye nsanje ikukugirigishani. Poti 2019 mudzakavota nokha ena sadzavota nawo tidzakuonerani ndi mfundo zZANUmukuba kKuDPP zo. Wokuba Toto, aayeee…..okuba toto, ife takana. Okupha toto …..nanga mr cashgte aja amafunako chainkunsanja kuja.

#DzukaniAmalawi
#DzukaniAmalawi
5 years ago

That’s dale for you Kaliati. remember you were part of similar plans against MCP. Let’s not condemn things that we were part of hardly a few years ago. focus on delivery of services and development to the people of Malawi and then you’ll be rewarded accordingly. Kuyalutsana will not help any one.

Masoambeta
Masoambeta
5 years ago

A Kaliyati koma aside kumatulwana anthu pa misonkhano ya UTM. People want to hear ma plan a dziko osati kutonzana all the time. Let’s make the change and practice mature politics.

Neno
Neno
5 years ago

ZAKAKUBVUTANI KUMENEKOOOOO….APUMBWA INU.

Amdala bambo
Amdala bambo
5 years ago

CHANGE !!! CHANGE !!!! I SENSE CHANGE

Chemjambe
Chemjambe
5 years ago

Komanso DPP mwafika pauchitsiru bwanji mpaka ma strategy ake amenewo ? zomvetsa chisoni bwanji
This just shows that the president is truly surrounded by cowards, dunderheads and bootlickers etc.
Now you are turning to beer to solve your problems eish SHAME!!!!!!!

Read previous post:
Mutharika says Brics summit beneficial to Malawi: To tap in US$34 bn pool for infrastructure development

President Arthur Peter Mutharika has described his trip to 2018 BRICS Summit as beneficial to Malawi's infrastructural development. BRICS  -...

Close