Email a copy of 'Kaliwo to grill Chakwera in court over MCP convention' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
newest oldest most voted
Notify of
moyo kuwawa
Guest
moyo kuwawa

Satantana ndiwe moya wa chabe chabe nzeru ulibe

phiri
Guest
phiri

I want people who can lift the party up not praying dada in the 18 yards box.You want us to loose this Golden chance ,go and wait aside.

Hatton
Guest
Hatton

Bwana Kaliwo, mwai uja wafika tsopano. Umpanikize mkulu amenyo ndi mafunso. Pamafunso amenewo osaiwala nkhani yokuba madzi yomwe ikudetsa mbiri ya kongilesi. Osaiwalanso nkhani ya nyumba yakumaula yomwe komwe kwachokera ndalama zogwilira ntchitoyi sikukudziwika. Ndi njira yokhayo yomwe akuluwa angachotse mmaganizo a amalawi okaikira kuti mwina ndalama zomwe chipani chimalandira kuchokera Ku boma ndi zomwe zikugwira ntchito imeneyi. Maganizo ena omwe a amalawi Ali nao oti mwina a Gupta a ku Malawi akumawagwira dzanja bwanawa achokanso. Bwana Kaliwo, osamuseweletsa mkuluyu, mumpanikize zamphamvu.

Kaitano
Guest
Kaitano

Kanundu kikkkkk, inu tumizani A.C.B not Kaliwo, kodi umbuliwu bwanji? kubadwanawo eti? the Water from the main Pipe up to the Meter is for Water Board, after Meter to the house where ever you may take it is for yourself, this means illegal connection can not be from the Meter to your house but from the main pipe to the meter, now if the water has been connected illegally from the main pipe to the meter, you can be having bills, after meter their is no illegal connection because it will be charging you. Why do we have bills while… Read more »

Putin
Guest
Putin

Zingobwirani mankhwalawo basi. shupiti

nzeru nkupangwa
Guest

Sizikugwilizana. Nenani mfundo. Mankhwala ndani samwa?

Simon mvahe
Guest
Simon mvahe

Zimwani makhwalawo Kk kkkkk paja amazunguza mutuuuu muzidyanso nsima kwambiri. Zandalezi zikuphaniiii

Chilungamo
Guest
Chilungamo

Bwana Kaliwo may be a fine lawyer, but politically he now realises he guffed big time. He knows, politically he will be completely useless and irrelevant after MCP convention. Finished ngati katani. And his recent political stanzas are but last kicks of a dying horse. Unfortunately it’s too late for him, He should have known better. One cannot serve 2 masters at the same time. Good lesson for other political wanderers.
Nkhanga zaona!!!

santana
Guest
santana

Mr Kaitano, which is painful to lose a mere by-election and a 50+1 which was connected to win the 2019 general election. I ask you Kaitano and your MCP to test the waters in the south by winning the two coming wards in Mangochi and Mulanje. We told you that you should have boasted if you won strongholds of UDF and DPP. Now the test has come for you to prove to Malawians that you have penetrated the strongholds of the two parties in the south. @Cadet, which Chakwera is being made king by divine process? Was he not there… Read more »

Kaitano
Guest
Kaitano

Hahahahahahaha Mr Santana, 50+1 was not for M.C.P!! it was for Malawians, kodi simuva pati? kodi do you have MPs in every District? if so it means kulibeko zipani zina which i believe it is not Malawi then.
In a country where there is Mart party system, you will not have and it will not happen i repeat it can not happen having M.Ps from one party, kaya zimenezi mumazidziwa? this means we cant not have M.C.P MP candidate every where so as D.P.P….. kaya zanveka kaya, ndukayikaso pamenepo.

Mona
Guest
Mona

Santana ulibe nzeru

Kingsley
Guest
Kingsley

Santana wadinda mfundotu apa ndipo ali ndi nzeru. Opanda nzeru waoneka.

Joseph Banda
Guest
Joseph Banda

thats the way to go mr kaliwo,,, this thing chakwera should go back kuubusa anathawako, kkkkkk

Achi
Guest
Achi

If Kaliwo was sane and a true custodian of the MCP constitution he would have turned down the appointment by Chakwera as SG and asked for an emergency convention. It was Daza who was elected as SG while Kaliwo was but just appointed. One thing the nkholokolos hate Chakwera is due to his bravery to call for fresh elections for all office bearers across all MCP structures which resulted in most old guards losing to new and youthful blood. It was therefore easy for the kholokolos to mobilize innocent but disgruntled old guard for the kholokolos selfish ends. On the… Read more »

Mfumu yopanda madyela
Guest
Mfumu yopanda madyela

Achi you can analyze issues. Now what baffles me most is the character of this selfish Kaliwo. Surely uyu ndi mmodzi mwa anthu aja olanda ufumu usali wawo. Koma chifukwa choti they were asked to help basi kuyamba kudzimva. But MCP is too big for Kaliwo. This guy by the time he realizes the fight was too big for him he will be completely battered. Munthu omvetsa chisoni, osatha ntchito, osayamika, namadanitsa komanso mvundula madzi wachabe chabe. He is very ungrateful. I hear he has never been to a meeting that he himself calls for it and never sent apologies… Read more »

Mchape
Guest

all the way Chakwera and Mia pa ballot what a team

Goliati
Guest
Goliati

Zikomo kwambiri a kaliwo poletsa convention, zimene zikuthandauza kuti a chakwera akhalabe pa mpando wawo mpaka pamasankho ndipo Alonso ndi mphamvu zosankha running make wawo, Ife zokanganazo tilibe Nazo ntchito Juno Ku brach ,area and all Malawians needs MCP to rule , kaya chakwera kaya ayi, amalawi taona maboma onse .DPP yalemba mmadzi with their propaganda yawo ,mukufuna kutindiuza kuti Ku chipani chawo kulibe kulimbana?

Haston
Guest
Haston

It’s unfortunate that some people are connecting every mess in MCP to DPP machinations. Okay, if we say it’s DPP who are behind, let’s look at it this way. You are a husband, and every time you are at loggerheads with your wife, Then you accuse man X to be behind your squabbles. This happening for years. The question is, between you and man X, who is weak here?. Dolo ndi ndani pamenepa?

Kaitano
Guest
Kaitano

Dolo ndiwe

nzeru nkupangwa
Guest

Dolo ndi DPP ENANWA MANTHA AKUWACHULUKIRA. LET THEM SORT OUT THEIR MESS

Mfumu yopanda madyela
Guest
Mfumu yopanda madyela

KUDZINYENGA NDI CHALA UKU

Mfumu yopanda madyela
Guest
Mfumu yopanda madyela

A good example but not relevant to this issue. DPP’s style of governance is divide and rule. Uwuwu si udolo in anyway. A brave leader lets his actions to speak for him and not cause commotion to his competitors. Pofuna kulanda mkazi wa mwini sutuma anthu kumakagenda padenga pa nyumba yanzakoyo, koma umatchaya mfundo zako kwa mkaziyo kuti azisanthule yekha.