Email a copy of 'Kambalazaza challenges Malawi govt on economy' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

68 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Phi mike
Phi mike
8 years ago

52 I think this is not the best way to comment. Don’t pipo have freedom of expression? Ndinu achitsilu mwamva! Backward pipo.

victim Chamkhuni Lwazazi
victim Chamkhuni Lwazazi
8 years ago

Malawi is endowed with vast resources but are misused and untapped while their values are dwindling at world market. did we know that fossil fuel and gas are now dwindling in returns at world market favoring on the rise solar and wind energy sources? Yet we have been exploring these resources for years and years while the nation is getting poorer and poorer. Tanzania is now extracting gas near Malawi where there is a ground strata of the gas piping it to Dar es Salaam where it is stored and distributed for use. Extraction from from these strata means even… Read more »

Emmanuel Brown
Emmanuel Brown
8 years ago

very good bishop,apa zinthu tizivomerezako zavuta ndithu

clement
clement
8 years ago

Iwe fisi ukuziti dobo. Ine zomwe ndikunena sizankutu ndipo ndimayenda siphwii malo amodzi kumaswa Ana ayi ndipo ndimawerenga nkhani za Maiko ambiri wamva. Ngati umphawi wakuvuta ungofa ndipo ndiwe mzika yosafunika yopanda ntchito, bulshit.

DOBO
DOBO
8 years ago

No 56 ndi wabodza loopsa.Zambia kapena SouthAfrica iti?. Bodza lotcha nalo mzikiti limelo.Munthu wa nzeru zake ungayerekeze Malawi ndi SouthAfrica.Ndiye u DPP wo wawusapoti mchimbulimbuli.

DOBO
DOBO
8 years ago

Inde,inde Archbishop lankhulaniko .Akakhala mabishop azanu adalowa mchala,adayamba mantha. Nanunso masupporters a DPP mungokhalira yotukwana ndi kunyoza pa social media. Munthu asadzudzule boma kapena DPP. Ndi mtundu wanji wa anthu. Kungokhala ngati agalu achiwewe. Usapota usavage umeneyu.Pali chifukwa chomatukanira munthu chifukwa cha Maganizo ake.

Bulutu
Bulutu
8 years ago

Kuyenda mbali bwanji?

From donor aid to zero aid budget.

Rev
Rev
8 years ago

Vuto lomwe anthu ambiri amakhala nawo ndikusanvesesa nkhani, munthu aliyense ngati mmalawi ali ndi ufulu opeleka maganizo ake za mmene dziko likuyendera, Abishop sakunyoza boma ayi, ndipo sazanyoza boma lililonnse, musamapotoze mau ayi please please, iwe awlemba nkhani iyi ndiwe waboza, stop

maganizo
8 years ago

first of all we need to get together and unity and get rid off greedy shellfish mind we always have and be creative to initiate something for the benefit of all as nation..thank you

Binton wakale
8 years ago

Timafuna maso mphenya woterowo koma umodzi ukufunika kuchita chinthu limodzi ndipo pa nthawi yake.

Read previous post:
Namalomba heading back to Malawi Revenue Authority

Beleaguered former Malawi Revenue Authority (MRA) Commissioner for Exports, Shadrec Namalomba, is set to go back to MRA where he...

Close