Email a copy of 'Kamlepo says Mutharika on countdown to go: Chihana condemns coup charade' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

27 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
BEN
BEN
8 years ago

i tell you dpp is scared,, why have i said
1. ikanakhala dpp ilibe mantha sakanamanga kabwira ndi anzake, chifukwa amene anawamanga siboma ayi koma chipani cha dpp pogwiritsa police
2. akanakhala alibe mantha sakana sonkhanitsa mafumu kuti atsutse . mafumu athu ndi opusa chifukwa sadziwa kuti iwo they belong to state of malawi , and they are above govt. they have to defend anthu akumudzi osati anthu ochepa
3 pomaliza upresident siufumu. abale anthu anayesetsa kuti akhale m’bomo to cover their criminal activities. dont you notice mafia like activities in dpp,, you will yet see. ACHOKE ! SIUFUMUTU UWU

Walhelha Ochavo
8 years ago

MCP……MCP……..HOOOOO simudzalapala ndithu ,after all kodi silver jublee yokhala ku opposition mukondwerera liti? musayiwale kuti kunali obaba,lero ali kuti? SECTION 65 NUMBER ONE….BUDGET NUMBER TOO.do you think zimene mukuchitazo anzanu ndiye ali mtulo? you are just wasting your time? mukuganiza kuti ulendo uno boma muloweranso pawindo? zomwe mukuganizazo mchimodzimodzi munthu amene akukwera mu mtengo akunyera kuti potsika adzazipaka yekha!!!!!! watch out!!!!!!!>>>>>>>>>>>>>>

Dambudzo Chihana
Dambudzo Chihana
8 years ago

Kuzolowera kulowa m’boma pa window.mukuwona ngati akapanga resign ndiye mukhalapo?mwawuponda.2019nso muzaluza with distinction abusa amkhwidzi inu.MCP,PP, ndi AFORD?nkumati muzapanga boma 2019?mukazawina muzandifunse

Well wisher of malawi
8 years ago

A mcp,ppp ndi afford,you cant remove one from seat because he has weakness,the way you are behaving,you are completely displaying your weaknesses.idont know, with your theorogy doctorate,do you read the bible?,all leaders had weaknesses ,if you are one who put him on the seat mumuchotsa,ngati its God you wont,and inunso pansi pamtima wanu you know zimenezo,everybody has weaknesses,mukakhala inu bwenzi anthu akukulozani zala,pano u say azanu akulephera inu mukukhoza?

wakum'mawa mario
wakum'mawa mario
8 years ago

Akamlepo ndi anzanu a chakwera mumamudziwa nyapapi? inutu mwachepa mukunama ndipo mundikhulupilira mlomwe simungamuthe kagwereni uko!! munayambira nthawi ya bakili mumati mulowa nthengo , munalowamo? mumafuna muziopyeza kuti ena aope angakuopeni ndani inu? mwauponda mukhaula!!!!

mjomba welewo
mjomba welewo
8 years ago

Some one used to “Malawi woyeee….!!! people could respond woyee….!!!” but in actual sense …he is siphoning billions of kwachas and building huge mansions. Ndiye akanakhala Kamuzu bwenzi akanamanga the tall buildings as of that twin towers of USA.The first role for the ACB boss after being appointed by Public Appointment Committee of parliament is to clear all milandu yamgonagona, MHC scandal,k577 billion scam, green belt project tractors and that of Njauju…Malawi want to know all of that…Chakwera woyee….!!! Chakhwantha woyee…!!! wina atuluka thukuta nkamwa…..

CHAMBE OR CHAMBA
CHAMBE OR CHAMBA
8 years ago

Garbage in garbage out. I have never heard so much nonsense spewed out from one man like one person named CHAMBE. CHAMBE honestly you stink. You are the type that make Nyasa readership so boring. Your comments are so inept and lack intellect. why do you always comment Eish! Whatever DPP/Bwampini gave you, you must be a millionaire. If not then shut up your stinking beak for once. CANT YOU MAKE ONE BALANCED COMMENT FOR ONCE. THIS IS NOT A DPP PAPER PLEASE!

Myao
Myao
8 years ago

CHAMBE-AM SURE NDIWE CHAMBA- DO YOU KNOW THAT EVERY BIG JOURNEY STARTS WITH A LITTLE STEP, LITTLE HOLES CAN SINK A WHOLE SHIP?? STUDY THE POLITICAL TRENDS IN MALAWI THEN YOU WILL UNDERSTAND HOW ANGER BUILDS UP IN MALAWIANS- I THINK WASUTA OF UR AN INFANT!!

mjomba welewo
mjomba welewo
8 years ago

If the Public Appointment Committee of parliament can be given that task of appointing the ACB boss as well the Auditor General this Malawi will develop at pace of Kamuzu…Peter Chakhwantha and your freinds you derseve something from…fight for the betterness of Malawi…K577 Billion scam ija tikufuna itheke basi …those who are involved should also be jailed no matter what immunity they have.Chakwera…..Chakhwantha…..and all your team at the opposition fight 4 Malawians …

Awa
Awa
8 years ago

Achoke basi.

Read previous post:
Chikadya defends retrenchments:  Blame Malawi ailing economy, not me!

The Managing Director of Times Group took to Facebook to defend his company’s decision to retrench nearly 70 employees saying...

Close