Email a copy of 'Kananji ‘deserves to stay on’- Bullets' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

32 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Stecy
Stecy
9 years ago

zimenezo nde ndizopuusa kwambiri. Konseku komwe wayikankha team yathuyi, kukonda ma foreigner bwanji instead of kutukulana

Luke kasese
9 years ago

kungofuna kumutchukitsa munthu kut watengetsa leag pamene ntchito yonse wagwira ndi kananji musiyen m’ brund azipita holiday yatha asakomedwe kuno. Ine ndi wa nyerere

lamuse
lamuse
9 years ago

Kananji ali bwino kwa mbiri timusiye ayitenge team yathuyi osati mabodza enawo.

Manyi sabedwa
9 years ago

owo pangan manyiwo ife titenga mwala okanidwawo

austwell
9 years ago

kananji woyeee!!!

austwell
9 years ago

more fire kananji,,.

democrat
democrat
9 years ago

If BB succeed dis czon it’s simply bcoz of Elijah Kananji & not de so called Ramadhan! Pauzimba sizoloredwa ngakhale pang’ono kushomola nyama yomwe wapha mzako!!

Kennedy Nthukwa
Kennedy Nthukwa
9 years ago
Reply to  democrat

Tiyeni tiupeze maullee!

lester mo
9 years ago

KANANJI YEMWEYO ALI NYATWA GUYZ INU MUKUONA BWA???????????????????

Kasiya boy
Kasiya boy
9 years ago

Ine ndi wa nyerere koma palibe chifukwa chomveka kuti mungalembere ntchito mbulundi pamene team waipeza atakonza kale kananji kodi amalawi tinakhala bwanji nsanje? Ndikananji yemweyu akhoza kudzakocha frames mtsogolo simukudziwa? Kananji mpatseni ntchito nexst season osati ngatiso othandizira ayi

AMANAH SUMANI
AMANAH SUMANI
9 years ago

KANANJI YEMWEYO ALI BHOO

Read previous post:
Female lawyers in justice delivery in Malawi

There is an apparent lack of recognition of the important role that female lawyers play and can play in justice...

Close