Zitsiru za makochi! Kanyenda, Fisher kuwafuna lero mutaononga kale zinthu! You can’t win titles with kids. Tinaonera Arsenal. Nine years playing good but no silver ware. Yes! you have to learn that experience is a good teacher
Anonabhani
9 years ago
Ndi ma professional abwerawa tanyadira kwambiri. Komanso the coming of Ficsher into the squad. Kumtimaku kuti mbeeeeee, ngati taponda mu ufa.
Apa ndiye ku wina kulipo basi.
why not including:james sangala, moses chavula, lucky malata,
Living chiukepo & nyondo its a suicide for malawi
koma mulimba ndi bwana keita akubwerawa
lets pray hard
coz adachinya agaInst kinah phIrIs team mwatI basI ndI profe za nziii
lets hope for the better
You journalists need to check caf rules. Malawi is not on position 4 but rather position 3 because of better head to head record against ethiopia
Koma kanyenda akatithandiza?