Email a copy of 'Kapito blast ‘clueless’ DPP govt: ‘Maize scarcity shame to Malawi’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Kapito blast ‘clueless’ DPP govt: ‘Maize scarcity shame to Malawi’' to a friend
Malawi’s acoustic icon Giddes Chalamanda’s childhood dream to perform in the United States of America is steadily coming true as...
Chimanga chinapita ndi DPP. Ayenera kusintha Makaka amenewa. Mbuzi Zokhazokha, mano omera kumwamba. Ndizimenezo poti kampeni yanu inali mipingo, mwagwa nayo. Ana anjoka, akalijosolo.
Uncle Kapito.
Don’t stress Yourself. Fold your Hands, close Your Mouth.
Rest comfortably at your Home and Family. Take a Glass of Soft Drink, drink basi.
You have Spoken, Advised, The Whole World gives Testimony.
Just Leave Open Ended.
We are not created to suffer.
God will Sort Out.
Kapito u r just wasting ur energy talking za abwanoni awa.samamva sazamvaso ndipo sazathekaso.Anyway i dont blame them,i blame those who put them in power.
komanso sikuti ngati munthuyu ali mulomwe chikhale chitozo kwa alomwe onse it doesnt work like dat guys lets be honest sikuti akumpangisa ndi alomwe enawo kt zinthu zivute pa malawi
kapito is not a liar bcz panopa anthu chimanga akuchigula pa MK15000 ndie enanu mukuti chimanga sichikusowa wat do mean bwanawa zinthu zangowasokonekera basi kukanakhala kt udindo amangotula ngati bawo bwenzi pano tikuti atula pansi bcz zawakwanatu ma bill a magetsi ndi awanso akwera kusonyeza kusaenda kwa zinthu pompanonso mumvako kt mafuta akwera anyway asova poti anachita kulembetsa
Eeeee mukutsutsa chifukwa mukudya kasanu pa tsiku, ndalama za cashgate zili mmatumbamo, palibe chimene mukusowa… Zoona mavutu ali mMalawi munowa wina nkumatsutsa??? Koma Mulungu akuoneni ndithu. I thank you so much Mr Kapito for speeking for us the voiceless, I hope government could listen and act immediately before we loose more lives…
Kapito thinks he is more intelligent than everyone else. He is just noisy and self centered.
Nthawi ya Joyce Banda kunalibe izi. APM is a failure
Part tym preacher, you are really very shallow. This govt told all of us that there was plenty of maize. Even some of its ministers started boastfully to buy maize and distribute it to their respective areas. All the govt needs is to whip up Admarc and sack those stealing maize to sell to vendors. Act on Admarc. Why no action? Is it because the so called vendors are actually dpp gurus in disguise buying maize from the Admarc backdoor and selling it through so called vendors at obscene profits. So act on your dpp gurus as well. Lastly where… Read more »
Alomwe mudziyankha munthuyi munamukumba kuti?