Email a copy of 'Kapito blasts Escom: ‘Refund consumers when there is balckout in Malawi’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

63 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Amalawi tiyeni tilimbe nazo zonsenzi ndi Mr MEC
Amalawi tiyeni tilimbe nazo zonsenzi ndi Mr MEC
8 years ago

These black outs are nothing but a strategy to sell Escom. Its a scapegoat. There is no money to plunder as the donors are tight with their money. What else can they do apart from finding faults in services then selling them. They sold the Bank and they confirmed that they don’t know what to do with the money. That is if the money is still there. The Mortuary’s are not working and the solution is to sell them. The Hospitals are non functional coz of lack of drugs the solution is to sell them by oppressing the poor who… Read more »

Bahasa
Bahasa
8 years ago

Kuvuta kwa magetsi ndi plan ya boma tidziti Escom yalephera ndiye tipeze strategic partner cholinga agule company

vyaya
vyaya
8 years ago

I thought Kapito you said JB knows nothing? Lero???? You supported this clueless professor just for being your tribes man! He sold MSB for a soing, you didn’t match, blackouts everyday, you don’t match, forex skylocketing,you don’t match in short everything in Malawi since DPP came to power is not working,,,,why are you not matching everyday as you did during JB? And this CAMA is it a life time position for Kapito only? You preach democracy, and why are you not retiring from CAMA? Even you since you became CAMA president, the plight of consumers is becoming worse and worse,,,is… Read more »

MLOMWE2
MLOMWE2
8 years ago

A ESCOM NANU MWANYANYA MA EXCUSE A BOZA MUKUNGOTHAIMA NYENGO IKAKHALA NTHAWI YAMVULA MUTI MCHENGA NDI ZINYANSI ZAZAZA MUMA TUNEL NTHAWI YA DZUWA MUKUTI MADZI ACHEPA NDILITI POMWE. MUZAKHALE OPANDA VUTO?TIUZENI ZOONA OTHERWISE YOUR SERVICES ARE VERY POOR MWINA PADZIKO LOLONSE LAPANSI. PLIZ WAKE UP!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

MLOMWE2
MLOMWE2
8 years ago

A ESCOM NANU MWANYANYA MA EXCUSE A BOZA MUKUNGOTHAIMA NYENGO IKAKHALA NTHAWI YAMVULA MUTI MCHENGA NDI ZINYANSI ZAZAZA MUMA TUNEL NTHAWI YA DZUWA MUKUTI MADZI ACHEPA NDILITI POMWE. MUZAKHALE OPANDA VUTO?TIUZENI ZOONAOTHERWISE YOUR SERVICES ARE VERY POOR MWINA PADZIKO LOLONSE LAPANSI. PLIZ WAKE UP!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

Gift F Nkupusa Brown
Gift F Nkupusa Brown
8 years ago

Pakufunika kuchosako onse, MAGUYZ AKU ESCOM AKUJAILA HEAVY, TSIKU NDITSIKU BLACKOUT, MA BILL KUMABWERA OKWERA, KODI MANGOFUNA NDALAMA NTCHITO SIMUKUKWANITSA, NDIKUPEPHA A KAPITO MUONE BWINO BWINO NKHANIYI MUSAWASEKELERE AONONGA MALAWI, KUPMPHATIKIZAPO MA COMPANY AMAYIKO ENA SANGABWERE KUDZAPANGA BUSINESS KAMBA KAVUTOLI,

Kaziulika Chimugonda
Kaziulika Chimugonda
8 years ago

Nyasa Times, investigate what my colleague from Zobue Mozambique has told me today. He says, Zobue is using electricity from Malawi. He furhter said, their blackout is once a week on Thursday. Is this true?

Hoitty
Hoitty
8 years ago

Water levels are low during DPP rule only??? Kodi mu January sitinakhale masiku ambiri opanda magetsi kamba ka mavuto obwera chifukwa cha mvula yochuluka?

MWAPIYA MULHUPALI
MWAPIYA MULHUPALI
8 years ago

Iwe Mbwiye Kapito, Management Sabotage Ya Chani? Apa Ndiye Pakuwonetsa Kuti Alhomwe Inu Luntha Palibe. Management Yimapanga Magetsi? How Do You Expect Things To Improve When The Little Financial Resource Escom Is Generating Bwampini Is Looting.Vwampini Put A Board There Brimmed With Politicians Who Knows Nothing About Power Generation Or Administration.They Are There To Milk The Escom To Prop Up The Clueless Bwampini Adminstration You Shamelessly Supported And Voted For.Escom Needs Forex To Import Spare Parts, Equipment,Transformers Which Elsewhere Is Being Manufactured Localy.But Mbuye Wako Bwampini Quotalized Tertiary Education How Do You Expect A Country That Promotes Mediocrity To Develop.Kapena… Read more »

Joseph Moyo
8 years ago

aKapito nso penapake muzilankhula ngat mukulankhula ndi anthu ozisata much of ulamuliro wa mai ndidali ku ntcheu long lakeshore koma ndidakhala ndikuzunzka ndi ma blackout simatha sibata ndye mukut chiyani.ndiku bt sindidakhalepo ndi black out for2dys.mumasusa njira yabwino escom idayenela kugulisidwa kut izipanga za kupsa after all singakwnise kupeleka mphamvu zot zigwirisidwe mu migodi yomwe tikuiyembekezera kuyambai.mumaopa kugulisa ma company koma Grain and milling ataigulisa pano ija ikuchitabwino.ndipo yalemba ntchito anthu kuposa nthawi idali yaboma.akapito khalani serious simunganene kut nthawiya jb idali bwino ndikukhulupilira kut ndaramanso zidaonongedwazomwe zikupangisa mavuto wa.tiyeni tiuzane zoona.

Read previous post:
PP’s Mwenye quits over ‘leadership confusion’

Former ruling People’s Party (PP) Director of Social Affairs Steven Mwenye has resigned from his position and has immediately withdrawn...

Close