Email a copy of 'Karonga Council staff threaten strike over meagre wages' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Karonga Council staff threaten strike over meagre wages' to a friend
Lilongwe Senior Resident Magistrate Patrick Chirwa has ruled against State’s application to confiscate property owned by two Cashgate convicts Victor...
New revelation: wagulisa male mu bus depot kwa Jones Kalambo ndi Kayisi pa malo poti mpokanizidwa ndi a physical planning. Komaso akufuna kugulisanso kunja kwa bus depot koti Local Gvt yinapangapo kale operation dongosolo. Akuti zonsezi akupanga yekha ndi a Chair osapanga consult Planning Department kumene kuli ma Physical Planners, Lands ndi a Estates mgt
Kodi anyamuka liti Rosemary kukagwira ntchito yake ya uheadteacher? Local government is a funny ministry. It is fond of misusing human resources. Resemary is a relation of Christopher Makileni. Mwina zinthu zisintha poti Makileni anamthamangitsa. Galu wamunthu ndiye anatibweretsera Galu wa Dc ameneyi . We want a professional DC here apo bii tiwonanenge
Uyu Rosemary akuti talks bad of Emmanuel Bambe becoz staff talk good of him while he was DC in Karonga. Panga zako anthu adzakuyamikire!!! Unapangitsa mwana Chisuse kupempha transfer kupita ku Nkhatabay chifukwa cha nsanje atagula Minibus from his Rice business
We understand she likes miseche too much. Signs of inferiority complex. She has no confidence in herself. Kodi mwati wasinthaso driver?
Osamunyengelera coz wazolowera , timupweteka otherwise w need salaries, zausilu w r tired of her tendency of not resPecting direct employees . If she will not die for the sin , she will surrender. Ask your collegues will help with a gud advice remember w had CHIZANADI CHIRAMBO and who are you. Waba ndalama ndipo a ku accounts ndi khalidwe lo casha ma cheque a fuel in the name of FOR STAFF, MAKILENI CHRISTOPHER mayt god. Punish you for the burden u brought on us , National audit where r u,ACB , Local GVT do something otherwise kutowniko abwera mu… Read more »
Anthu apa Karonga amakonda kumwera salary yonse Kangala ndikudyera Susa ndi Ndoki.Nikuwanya chomene Wankhonde.
Kodi adakali konko? I mean uyu Rosemary… Anamupatsa kale kalata ya chiwiri kuti adzipita ku Education kwake akagwire chalk. Pls KA guys munthuyu adzinka. Inde ndi wakwathu ku Dowa koma ndithakati, Hule!
Mwazgobera kulyera Bantu, mulije name son I. vima councillor navo vibulu vekhavekha no mbombo.
Madam DC, u say u dont recognise them at the same time u shall look into the matter.how shall u look into it when u dont know them.madam be careful because someone greater and bigger than u is watching from above,His name is GOD.
This DC is in good terms with our paramount Chief, No wonder tidakazuzika .
That’s not true kuti she is interms with His Royal Highness. Paramount doesn’t need this ugly woman. We understand she is very rude to Him. She doesn’t respect the Ngonde culture.