Email a copy of 'Karonga councillors boycott meetings, demand cashgate probe' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

31 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MERCURY
9 years ago

ATUMBUKA WOMWEWO, KUTI WA! WA! WA! MPOTO CASHGATE.com SOPANO, MWAISOVA KALE

goody
9 years ago

KUBA NDIKUBA KAYA NDI TAMBALAGATE,KWACHAGATE OR MAZIRAGATE.FUFUZANI NDIZIWE KUMENE MSONKHO WANGA UKUPITA INE MWINIWAKE NDIKUTUWA

Mkango
Mkango
9 years ago

Karonga District Council has lost it’s direction since the removal of our dear Bambe and Bulukutu, this woman without husband palibe chomwe amadziwa cha council. Kaya boma linamtenga kuti. Kubaso too much every weekend ku LLZ akuti kukapemphera. Plz councillors if u want ur district develop deal with mbuli iyi Rosemary. Council no direction

kamutondoli
9 years ago

Investigations should be done to : 1. District Social Welfare Officers and their Juniors in Mzuzu, amanga zinyumba ma kalaliki a ku Social welfare, agula magalimoto, ma workshop/trainings oyenera kuwachita run for 14 days amangopanga 5 days ndalama zotsalazo mmatumba mwao, komanso kumakhalanso ma ghost participants. Ndipo ngati kuli mbala zina mu dziko muno zagona ku ma ofesi awa: i. District Social Welfare Offices, muone from Chitipa, Karonga, Rumphi, Mzuzu, Mzimba, Nkhatabay momwe maofesala ake agulira magalimoto, amangila zinyumba, amalandila ndalama zingati. Kamai ako kambala kadali ku mzuzu lero kali ku Headquaters kakudya za Cash Transfer tsopano. ii. Ma ofesi… Read more »

tonde
tonde
9 years ago
Reply to  kamutondoli

Nsanje galu iwe umafuna anthu amuboma asagule magalimoto komaso asamange nyumba.
Anaputa kusukulu ndipo mind a wawo ndi office.
Khala choncho kumawerenga chuma cha civil servants mxiiii

Munnyabu
9 years ago

We r always briliant and coragious see MCP founded by Oton Chirwa,multiparty Chakufwa etc now F. Audit by mkamwana JB, fedelism no need to mention taking to tasks DC simungawonepo vuto mbuzi inu za chabechabe akachirombo ka ku Dowa ndi alomwe mbuli

Kwangwagwa
Kwangwagwa
9 years ago

Pa Karonga apo mwatani. Mungowuwawuwa anzanu ku ma district ena akumaba zenizeni. Inu mukut 5 million basi mukuvutisana chonchi, asaaah! Imeneyo si cashgate ayi, koma tambalagate. Kikikikikikikikiki. Karomga woyeeeee! Nyungwe woyeeeeee! Bwiwa woyeeee! Mwanjawala woyeeeee! Mulinkafu?

Mkhalangeya
9 years ago

No comment. Kyungu usova wekha.

Aaron Msena
Aaron Msena
9 years ago

anthu osakonda dziko lawo inu!

MWENECHO
MWENECHO
9 years ago

This is what most stupid MPs do in Malawi. They don’t engage . I am one of the Councilors in Mzuzu City, but I don’t remember discussing anything on the relocation of CDF. The MP, Uncle jOSY is seriously misled by his campaign-time advisers . He needs a sober development team if he is to deliver. He must realize this is no time for jokes. Its time to drive development. The Youth are right, the resources were not spent on the planned and intended purpose. He and the clueless Mayor failed to think outside the box to deal with the… Read more »

C
C
9 years ago

Next ikhala Rumphitu ndipo ndisadzamvenso kuti mwamuitana nkumamufunsa mtolankhani wa ZODIAK ngati m’mene mwachitira pankhani yomwe anafalitsa ya kalondolondo wachitukuko cha nyumba za aphunzitsi! Sakunama ndinu mbava mapeto inu! Inu mumaitenga ZODIAK ngati state broadcaster??? Inu nyumba mwamanga ku Chiskemba zija pali chilungamoo????? Anthu openga mwapanga bwanji?

Read previous post:
Silver third-place bid collapses: Malawi TNM Super League

Silver Strikers’ hopes of snatching the third place from Blue Eagles have vanished into thin air after the Central Bankers...

Close