Email a copy of 'Karonga market shut down: Council force traders to pay revenue' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Karonga market shut down: Council force traders to pay revenue' to a friend
As the 2015 TNM Super League is about to kick off, private owned Matindi FM Radio has said it will...
musapereke ndalamazo ayi, zimapita kuti akachita makani a khonsolo memanani muotche ndi kuwagenda basi
An advice to all the market vendors in Malawi: Trading at council market is not a right. If you see that the market is not conducive to you, move on to a better market. You are not forced to trade in one market for life. Karonga council, use your by-laws to punish these stupid vendors. Close the market for a week adya matope amenewo.
Comment inu Atumbuka Lipilani rentals bwanji Kodi mtudzu?
Akukana kupeleka revenue wa ndiaku tanzania,matayifa sia malawi.ndiye kungowawuza kuti anyamuke basi
A Khonsolo kuba mavenda amapeleka misonkho tsiku ndi tsiku koma mukulephela kukonza zimbudzi, kuchotsa zinyalala mumisika yambiri mumaboma ambiri mdziko muno. Go hard wena Karonga. Ndalama zathu za matikiti zikupita kuti.
Fighting for my rights, do not step on my toes!
Amalawi mwafika penapake kodi ufulu wa democracy ndi umenewu osalipira msonkho
Mavenda inu ndi akuba mukufuna dziko lino likhale mu umphawi. stupid Venda pay tax nowwwwwwwwwwwwwww
More fire ma vendors aku Karonga. These assembly officials does not consider vending as a proffession, and yet they are renting in our houses. Ur friends in Kronga main market have shown them a yellow card. Next is Rumphi main market. All officials shall be shown a red card. They are so corrupt.
Tawapaseni boma lawo azikana kupereka misonkho awone ngati dziko lawolo lingazAyende lopanda tax.Zindere zakufikapo…
its the poorest of the poor who always suffer