Email a copy of 'Karonga village headman hacked to death: Witchcraft wrangle' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Karonga village headman hacked to death: Witchcraft wrangle' to a friend
Leaders in the northern region in the arenas of religion, development and social science, politics and activism have taken turns...
u r the next……I min u the pre………………….
No. 10 ndiwe onunkha kuujeni kwakoko. Mumene kumanunkhila kuujeni kwako ndi kwa mlomwe, muchewa, muyawo, mungoni, musena, mtumbuka ndi chimodzimodzi. Palibe zonyozana mitundu apa. Mutundu wina uli onse umapanga zolakwika. Ndi mtima wa munthu basi. Timamva kuti achewa aphana, a lomwe aphana, ayao aphana ndi mitundu yina yonse imaphana. Nkhani poti yachitika ku mpoto basi mumvekele atumbuka atumbuka. For your information, si mtundu wa chitumbuka wapanga zimenezi ndi ankhonde. U cant combine asena ndi ayawo kukhala alomwe just becoz ndi a ku mwela. Umbuli bwanji amangwetu. Its high time tikhuzumuke zomanenana mitundu.
Atumbula mwayamba kuphana nokhanokha vindere
LOPUSA NDIBOMA LAMALAWIIIII LIKUDZIWABWINO KUTI KUMALAWI KULI UFITI ,AND KULIBE LAMULO.NDE ANTHU AKAGWIRA OR KUONA MFITI ,AZITANA,? MUMADZIWA KUTI ANTHU AMBIRI AMWALIRA CHIFUKWA CHOLODZANA? AND MUKUDZIWA.MUNGABVE BWANJI INU MULIMWANA NDIKUKULODZERANI MAKOLO ANU ONSE?KODI KUPARLIAMENT MUMATANI? OSAMAONA KHANI NGATI ZIMENEZI? STUPID ! BOMALAMALAWI KOMA KUBA KAPENA KUONJEZERA MALIPIRO AWO.
Mtemi wipe out the whole village of Mwantende kwa Songwe.Yabania ikusu between Mwasulama and Mwangwala.Bikututamyaga bwila aba linga mubalekile ikisu.Banya Mwantende bikututamya twe banya Sakabanga kangi bikutukosya isoni.
chamba achinyamata mpaka kupha mfumu ????
This has nothing to do with a tribe or district! It Is the condition of the human heart, whose solution only CHRIST can provide!!! If everybody at individual level can surrender his/her heart to CHRIST, people’s behaviors at individual level will improve – hate will be replaced with love, forgiveness, compassion. The sin problem has spared no one, no district, no country. This time it is individuals in a village in Karonga, next time it will involve someone in Phalombe, Blantyre, Kasungu, DRC, Texas, etc. Those who read papers and watch tv and are objective will testify of the moral… Read more »
Ithnk the whole africa need death penaty once
Thats inhumanity not tribes wake up guys
LAST DAYS