Email a copy of 'Keeper Simplex Nthala not up for Malawi selection: Faces law suit in Mozambique' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Keeper Simplex Nthala not up for Malawi selection: Faces law suit in Mozambique' to a friend
Criminals in Mangochi district on Wednesday failed to steal cash amounting to K4.3 million as they could not manage to break open...
ZIBWANA BASI.
Nanuso kukatengera zija mumachita kuno ku malawi kupanda ref you must understand foreign laws and apply them
Let’s just increase sporting academies I hope on a single year we can see some competition
ref kulandira ban kkkkkkkk!
a malawi kumachenjeradi tizitibulakodi apwizikizi kkkkkk ndanva bhoo
Let’s use those goalkeepers who are free. Komanso a FAM avenger chitsanzo kuti ngati Ref wayambisa chisokonezo azipasidwa chilango osamangofinya ma team. Sha!
FAM ndi a traffic police atihu simukusiyana..amathamangira kugwira wa minibus popeza amaziwa kuti atsutsa mosavuta ..ununso mumapeleka chilango kwa ma team kuleka ref. yemwe wazetsa chisokonezo kamba kosaziwa bwino ntchito yake poziwa kuti timu imakhala ndi chithumba than ref..zautsiru takutoperani
Anzathu Kumeneku amatha kumpatsa ban referee kani. Koma kuno amangoimbira za mbwelera palibe chochitika, koma ma team ndiye kwakhomelera kwambiri
Why did assault the reffaree?
Mwambo mwambo!!!!