Email a copy of 'Khumbo Kachali poised to launch new party, dumps PP again' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

21 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Kalekeni Kadzionere
6 years ago

Za ziiiii
zipani zonse mwapondako, chomwe muzaudze anthu nchiyani? Bwanji osangosintha chipani nkulowa china, ndiponso ngati muli ndi luso lotsogolera dziko bwanji osaonetsera kuchipani komwe muliko. kadziko kabwino kathu ndipo kakhoza kukongola kuchoka karonga mpakana Nsanje, koma mwakakhwasulakhwasula katheratu chifukwa chaumbombo kufuna kudziwika. Atsogoleri azipani zotsutsa boma akungopita komwe fungo

pixy
pixy
6 years ago

A khumbo khalani waka pasi nakurya ndalama zinu other wise you’re just wasting your time thinking of forming a party.Mubwenzenso mak50 aja munkapempha poyenda bawo pa Mzimba Hospital.

Banda
Banda
6 years ago

Akuluwa ndiodzikonda kwambiri ndipo ndiovetsa chisoni,amaganiza ngati mwana, anapatsidwa mwai koma analephera kuwugwiritsa ntchito.

Tiyanjane
Tiyanjane
6 years ago

Chipani chinyaki kuti chichitenji? Anyinu sonu akamba za kuyusa Aford kuti mpotu yiwele Ku regional block.

francis
francis
6 years ago

he is just one of these greedy politicians of the land koma sangapambane masankho

concerned citizen
concerned citizen
6 years ago

Do we have politicians in Malawi? I believe we have fortune seekers. If there are true and genuine politicians, may be very few. At the most, we have opportunists. Lord have mercy for my country

Konge Lesi
Konge Lesi
6 years ago

Komanso Atumbuka chimene amaganiza akasowa chochita ndikuyambitsa chipani basi. See Nyondo, Chiume, Gondwe, Kamulepo, Orton Chirwa, Aleke Banda, Chisi and many others. Maybe it’s high time scientists engaged in deeper research to find medication to heal the power appetite for Tumbukas. If truth be told, Khumbo Kachale is a spent force. Despite being vice president, he failed with distinction to eliminate the quota system

Harawara
Harawara
6 years ago

Malawians you don’t know Northern politicians. With the 50+1 system people like Khumbo, Junior Tzar of Aford and Ngwira are strategizing to be roped by big parties through party coallisions. They will form fake parties/groups and negotiate with DPP and MCP for posts in the 50+1 System because they know the system will force coalitions to occur for a party to win. The nomadic politicians are seeing this. So the parties being formed or reformed are meant to be tools to bargain for posts in the big parties. They know better than you do that they can not win on… Read more »

youna
youna
6 years ago

This man has nothing to offer Malawians. Ali ndi moyo odzikweza, odzitukumula komanso odzikweza kwambiri.

chaponda mchimanga
6 years ago

Osangolowa MCP bwanji? Greedy and selfish politicians of Malawi.

Read previous post:
Teen mum kills son, hangs herself: Another Malawi woman kill friend over cheating lover

A 17 year old mother in Mangochi has killed her three year old son by strangulating him and soon after...

Close