Email a copy of 'Lawyer Mbeta accused of bribing Malawi Revenue Authority officer -report' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lawyer Mbeta accused of bribing Malawi Revenue Authority officer -report' to a friend
For the past few weeks, the Twitter, Instrgram, Facebook, Whatsapp and the mainstream media have been flush with pictures and...
Kanyama, awa a case to answer wa sanamuphunzitse Frank. By the time Frank was ku Law School, awa anali atasiya kuphunzitsa.
Student of the guy who has a case to answer for conspiracy to murder. Ma graduates a University ranked number ninety-ninth.
mukapeza umboni oti anayenda ndi mkazi wanu mukumangowasiya? Why cant you plot just to KILL him. Ine sipangadutse mwezi alimoyo nanji ndimamwa nawo mowa sangalimbe amene zakuchitikilani hire me.
Kkkkkkk sindikkupanga nao
Malawi being ruled by fake lawyers including mwamuna wake wa Getu. Zotsatila ndi zimenezo. MRA CG your days are numbered. Ng’oma yolilitsa sichedwa kusweka
Choka iwe Mpopoma ndiye unamva kuti ma career enawa ndi ambuli?Basi ntchito kuloweza some Archaic Latin terms ndikuvala ziguduli zoyera anakupangani nazo colonise ma British?Ma lawyer apa university ranked 99th in Africa kuposedwa even ndi Mogadishu imene amaphunzira Ali shabaab ikunzumila pa zenela.What good can come out of it.Ntchito kukhalira umbava pamalawi to lead lifestyles that do not even match your genuine salaries.Malawi is sinking down on daily basis with that useless Unima mentality.
Maloya abwino alipo eg Mmeta he is superb.
Mmeta and several others.
Nsanje inu school ya uloya ndi ya anthu a nzerutu. Inu munali kuti ku phunzira. Asiye maloya a sangalatsidwe. MRA;AB are all corrupt including andale ambiri.
ASAAAAA…THIS WOMAN IN ZOMBA WILL NOT VACATE THAT ORDER. MALAWIANS ARE UNDERESTIMATING THE CORRUPTION IN THE JUDICIARY. THIS INSTITUTION IS SO CORRUPT THAT ONLY THE POOR CAN NOT GET WHAT THEY WANT. FROM MAGISTRATES TO SOME SUPREME JUDGES,MOST ARE ROTTEN! YOU WILL EVEN FIND MAGISTRATES CONNIVING WITH POLICE PROSECUTORS TO DISCHARGE SUSPECTS.
wawa bambo a chiwerewere a Mbeta. Mnchindo siunakukwaneni mwati muchinde justice?