Email a copy of 'Lilongwe Archdiocese launches Cathedral fundraising campaign, hits K43 million' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

1 Comment
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Damian
Damian
6 years ago

Ndikufunira akhristu onse a mu Lilongwe Archdiocese; nzeru, mphanvu, ndi chiwongolero kudzera mwa Ambuye Yesu Khristu pa ntchito yayikulu yomanga tchalitchi cha Cathedral kuyambira pano mpaka pomwe ntchito yayikulu’yi idzamalizikire. Komanso ndati ndipereke maganizo kwa Mr. Wilfred Dodoli ndi committee yomwe ikuyendetsa ntchito yayikulu’yi kuti mwina kukadakhala kwabwino kupereka bank account number kudzera mu nyuzi pepala’yi ndi njira zina zofalitsira uthenga, poganizira kuti pali ambiri akufuna kwa bwino, osati a Lilongwe Arcdiocese okha, omwe angapereke kangachepe pakufuna kuti zonse zidzathe mwa ndondomeko yabwino.

Read previous post:
Kamtukule appointed Shire River Basin project coordinator

Government has appointed Sydney Kamtukule as project coordinator for the Shire River Basin Management Programme (SRBMP) for its first phase....

Close