Email a copy of 'Lilongwe election rerun stay order extended until an appeal – Supreme Court' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lilongwe election rerun stay order extended until an appeal – Supreme Court' to a friend
For five months of 2014, two young Malawian girls—age 12 and 13—were forced to work as prostitutes in a Blantyre...
amene mukuti mcp singawine chisankho mukuyang’ana pati?Chisankho cha last year pa zisankho zonse tapanga munganene kuti chinali chisankho?It was pure drama.A chair kuvomera kuti pali zolakwika zambiri koma kulephera kupereka utsogoleri kuti dziko lidziwe zoona.And now we are plagued with deceit,corruption and mediocrity.
Ulemu Msungama is too childish to be an MP we cant allow it. He is a boy always on facebook. Whatever he does he announces on facebook. Even apeze nkazi he goes on facebook. He doesn’t work kudalira ndalama za brother wake yemwenso amadalira ndalama za nkazi wake. Pano ali busy ndi Nellie hule lomaliza ku Bt after atadyera atsikana ambiri. Duddy you just need to find a job somewhere. Za ndalexi ukule kaye.
a namasasu sanawine mpake mantha akuchuluka,munthu wachinyengo sasowa kuthamangila kufuna mboni mlandu usanakalowe.kuchemwetsela dala kuti aziti nthawi yatha kale ku masankho ena.ngongole yumuopsa.
Chilungamo chioneke apa.
Munaotchelanji warehouse ngati munawina. Ankaopa kuti ma presidential vote awoneka osiyananso. DPP mudzafa infa yowawa mbava inu
Wakana kukayezetsa akuopa chani? Singing
Our courts are really a disgrace to democracy. Corruption is very rampant in our courts and there are always questionable judgements. When are we going to dissolve our courts?
Owina anawina basi , kodi a Msungamawo analibe ma monitor? Apa akungotaya nthawi yawo , chachiziwikire ndi chakuti owina anawina , ukanakhala mpira tikanati replay match palibepo . Mwava a Msungama, zitayeni , kathu kasalako ati akamalize ndi lawyer.
Wasting time mind you MCP,DPP never fail and will never ever fail and what happened will happen again Namasasu is the winner.Big up Chancy Gondwe lawyer under KK Lawyers,you ‘re the gud example for all players REASON after kicking football you are still doing a very commendable job.
I think it would be wise to see the merit and de merit of the case, what are the facts, Namasasu anabela ma vote? or were the elections fare, incredible, transparent if the ans is yes why being afraid to have a re run? Id the ans is no why can people for once be smart? I think it is an open secret that the last elections which were chaired by mbendela have a lot to be desired? If one says MCP was bad I do agree it was bad and what it did is not good, but is dpp… Read more »