E-Mail 'Lilongwe man chops wife's hands, gets vigilante justice' To A Friend

Email a copy of 'Lilongwe man chops wife's hands, gets vigilante justice' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
newest oldest most voted
Notify of
kasisi
Guest
kasisi

Koma zinazi aaa kusowapo comment

Chilungamo.
Guest

apapa ayi mwamuna waonjeza. Kodi akazi muziwapanga chonchi? Kulakwatu uku. Kodi ngati zavutitsitsa bwanji oxangosiyana? Hey u man wait ur jehena!

chifundo
Guest
chifundo

This is wat we call nkhaza zophelatu, how can a real loving husband did this to a woman whom he considers a wife? Ufiti ndi umene wakula for sure. Malawians are known to be peace lovers koma izi zikutionongela CV as a nation at large, these pple need to b given coporal punishement

Odala Ochibwe
Guest
Odala Ochibwe

Bamboyu Waonjeza Koma Nkhanzazi Zikumachitika Mbali Zonse Amuna Ena Amakokedwa Maliseche Koma Samanena Choncho Ndipofunika Pakhale Lamulo Lokakamiza Mabanja Amene Amakhala Ndi Mikangano Kawiri Kawiri Azitha Chifukwa Zimakhala Kuti Nkhani Zawo Sizikutha. Kutero Nkhanza Zoterezi Zikhoza Kuchepa.Komanso Malamulo Alipo Amakondera Akazi Zimenezi Zikupangitsa Akazi Ambiri Kumapanga Mwano Kwa Azimuna Awo.Pelekani Ufulu Wokwana Kuti Amuna Azikhala Omasuka Kunenena Zomwe Amakumana Nazo M’mabanjamu!

Petros
Guest
Petros

Real satsanism

Frazer Pondiya
Guest
Frazer Pondiya

Lucky of humanity! Shiiiii up to hands cut off? GOD will punish u

Mong'onyolani
Guest

Apa cikuonmetsa kuti mwamuna ndi mbola koma mkazi ndiokongola….jelasi yakula kwa mwamuna. Anthuni Muonetsetsa

nkhedu
Guest

gud move

malawian
Guest
malawian

Mchdwa ameneyo

Austin Mussa
Guest
Austin Mussa

Owerenga khala maso Yesu Ali pafupi