Email a copy of 'Lilongwe Mpenu residents ignore voter registration, go for gold mining' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lilongwe Mpenu residents ignore voter registration, go for gold mining' to a friend
Feasibility studies are currently underway to determine the viability of a Graphite mine in Malingunde, Traditional Authority Masumbankhunda in Lilongwe...
Kani ZAMAZAMA ikuchitikans ku Malawi?
Anthu ukumba gold angamaoneke osauka chonchi
I can not see any thing like gold. koma atolankhani inu!.
Just go and open a registration centre ku dambwe komweko. Munthu wa nyau simungamuthe, ndi wamakani zedi.
Kusowa nkhani. Pali anthu angati pamemepa?
Malawi, no controls whatsoever. Where are the authorities to stop this illegal mining activity? Just sitting Phwii in your offices complaining about late fuel and accommodation allowances basi.
Zitsilu za anthu.But is the reporter not making mountain out of a mole hill? How many people in the constituency are engaged in gold mining?
Nanunso a Ku M’mwera. You think all who will register are for the thieving DPP, stupid UDF or useless PP? You are in for a big surprise.
MEC will always make sure that in all the opposition strongholds people are defranchised so that DPP can have an upper hand. This is deliberate and I guess the Commissioners have been promised big. This is exactly what Bingu did in 1999 when DPP won with a land slide some MEC staff was rewarded with diplomatic posts like Nankwenya and Bandawe while others like Lipenga was given the post of Director of Broadcasting at MACRA.
Apa ndiye ife a DPP plus UDF tidzawinadi shuwa. Atumbukanu yang’anani Afford. Siyani kudzikonda. Siyani kukangana nokhanokha.
Zisiyeni nyau za MCP zizidzola matopewo.
racism si ndiye imeneyo abwana… malawi ndi mmodzi tiyeni tikondane
Sorry anzathu a MCP ife kummwera tikalembetsa mwa unyinji ndikukabvotera wathunso mwa unyinji. Atumbuka chipani chanu cha aford ndiye dzikhalirani kukangana chomwecho anthu a chisokonezo inu
Shame on you pathfinder who always thinks of regionalism mbuzi mnthu okanika who is always bringing Malawi back
zoona Pathfinder,atumbuka anagulitsa chipani chawo cha afford kwa muluzi.Muluzi amawagula atumbuka 5 for 1 kwacha kkkkkkkkk