Email a copy of 'Lilongwe new club Cockpit introduces corporate ladies night' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Lilongwe new club Cockpit introduces corporate ladies night' to a friend
Officials from Malawi Human Rights Commission (MHRC) are seeking extra funding after the surprise and shock passing of Access to...
Mwina kuyetsetsako kuti nansongole ndi tirigu asakulire pamodzi. Nanga pa Malawi club iliyonse mutapite kumangokhalira mahule okhaokha. May I suggest kuti no one should be allowed in without a business card or some other proof of “corporateness”? Tatopa ndi mahule mma club ife. Mahule let them stay pa nseu.
this is commendable. let’s our ladies have space for themselves other than mixing with Yooz obwera ataledzela MA satchel. it’s will just be ladies uhule Achita ndi Ndanii. uhule ndi mtima you can do it even in church. green is 1000k very reasonable at a classic place like cockpit. kamweleni ku 18 ko mukadye kanjenya wa galu
Uchimo ukupitilirabe!!!!!!!
Zimenezi ndiye zimene timafuna mabumbs aja asokedwe tiyeni nazo koporate byching.
Tiyenazoni
This has shown that you ladies you have traveled to some countries, like here in Botswana Thursday is only for women having there time, i would say keep it up kutsukako azimai ubongo ndi kuwaphunzitsa some of good things, but am worried kuti zimenezo ndi u hule wakulau sizionongetsa mabanja yambiri poganiza ngati kuti they are there to do u hule? i can see wina akudulidwa dzanja ndithu.
Bar yanji Chill yomweyi mpaka K2000! Asa, ndizimwera pa Chesterfield kapena Watatu Pub ku Area 18B basi!