Email a copy of 'Lilongwe to host Intercity soccer Bonanza August 8-9: Nomads missed out' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
newest oldest most voted
Notify of
J . B .
Guest
J . B .

some of you people you are useless. Why kutukwana on simple think like this one? grow up guys. its never too late for you to change.

Dododo
Guest
Dododo

Neba pepa Maule ndi nyatwa…tatenga kale ka two miliko nanga si iwe ndi olemera kale….

Israel
Guest
Israel

Regionalism basi. What was the selection criteria? MOYALE bwa? Call it between Bt & Ll and not inter city.

nyakanyaka
Guest
nyakanyaka

chikho chilichose chanyowani imatenga ndi noma, ndiye afuna kuti ayeseko ena. mbite!!!!!!!!!!!!

Agriper
Guest
Agriper

Enanu ndi sanje basi bb iyamba kutolera twomi kenako carlsberg kumaliza ndi super league neba uli dyo ngat wadya chipwete cha lunda mapaz ngat kaligondo kaphovo wazii paife sudzawinaso khala ndikulemera kwako ife tizikukutha basi

Jaxxb
Guest
Jaxxb

The name is not right according to the teams selected. It shud hv been BB,Silver,Moyale&Red Lions. Not three teams from one City

Kin
Guest

Bullets Ndiyodziwa Masewera Ampira Kuposa Noma Ndiponso Ili Ndimasapota Ambiri Kuposa Timasapota Ta Noma. Ndiye Musamanene Kuti Bullets Ndiyosauka,bwenzi Italowa Mu CAF? NangaSilver Blue Eagles Civo Ndiosauka? Kungoti Akazathuwa Manoma Kulalata. Komabe Ukwati Wathuwu Siutha

yake ija.
Guest
yake ija.

Where is northern region please??? There r teams there kukondera basi!!!!

Mzaliwa wapa Nkk
Guest
Mzaliwa wapa Nkk

2million yachepa kwambiri zoyenera a Mphawi a Bullets osowa pogwira osati ife Noma takana zopusazo

Nasfam party acting president
Guest
Nasfam party acting president

Anasfam akuti : Bonaza iyi ndi ya anthu ovutika coz anadziwa kuti Noma singapite kumeneko. Du u know the cost? Fuel is MK200000.00 from n to, Kogona ma player n back staff fridy yofikira n satady MK 600000.00 food for three days Mk 1,200,000.00 game allowance for players n back staff for two games Mk 750,000.00. Medical first aid n refresher plus energise drink MK 70,000.00. It is almost MK2,820,000.00 so hu wil give extra money if u can win ka 2 millionko?. Chomwe muyenera kudziwa chakuti Bullets ikukakhala slave opanga ndalama za anthu basi poti ndinu osaona komanso aphawi… Read more »