Email a copy of 'Limbe back to business as shop workers get pay increase' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Limbe back to business as shop workers get pay increase' to a friend
The Lilongwe Magistrate’s Court has jailed former government accounts assistant Victor Sithole to nine years impronment for the so-called "Cashgate"...
Boma Lilowelelepo Pankhani Zimenezi
Nanunso ogwira kwa a Mwenye, Vuto muli nalo ndi lakuti ambiri mwa inu ndinu osaphunzira!! Ndiye palibe chifukwa chakuti azikupatsirani ndalama zambiri ngati munataya nthawi yanu ku sukulu chifukwa izi zidzapangitsa ana akubwera kutsogoloku kunyozera maphunziro poganizira kuti adzalandira ndalama zambiri kwa Mmwenye ngakhale osaphunzira!! Mwa a Mwenye momwemo alipo anzanu ophunzira akusangalala!! PASAVUTE, simunachedwe, ngati zikukuwawani, siyani ntchitoyo mukayambe sukulu ndipo pobwera uko mudzaona kusintha kwakukulu!! Inu mukuona bwaaaaa?????
pathako pako wamva
The most painful thing is that these Mwenyes bring in their dogs from India and pay them hefty salaries at the expense of local Malawians, yet their duty is being a guard. Mmalawi muno muli TSANKHO lomwe akupanga a Mwenye. Govt should engage researchers and find out what am talking here. If govt is really serious with empowering the locals, then let it start with dealing with these Mwenyes by deliberately giving more business tenders to the locals. By the way, if there are also govt department that don’t wish this country well, then it’s Immigration!!!! These idiots at immigration… Read more »
Does this mean Limbe Mwenye workers only or the whole country? I mean there also Mwenye workers at Maselema, Ginnery corner as well as Blantyre who are also eagerly waiting for the increment. For instance, there is a certain family turned into company firm that pays a worker K2500 per week and this translate into K10000 per month yet the owners are busy buying very expensive cars every two months!! I think it’s high time our govt intervene by imposing rules that can safeguard the locals from being exploited. If one feels can not manage to pay that much to… Read more »
KU LIMBE ZATHEKA NANGA KU BT SHOPS ZIDIKILENSO MARCHING?IIH KAYA MUDIKILE MUONE.
Increment for the all malawi business ppl y divideing in race
zinakati zizitere bwanzi zikukoma ndithu……keep it up.
Mwatasa ma burundi,mpaka kumapha amalawi
mumadikila alire kaye anthu nkupanga bwino act?
Aboma mutengepo phunziro apa.Why like ku Health,ma junior workers kuwapatsa malipiro ochulukilapo August ndi September then nkumati munalakwitsa nkuwadula mosaona kuti they are the lowest paid civil servants.
Kuwadula ndi zoona,koma momwe mukuwadulira is very irksome.Nearly 30%,that’s too much.
Boma limadandaula kuti maBank akumakweza kwambiri chiongoladzanja-then what’s this you have done.
I DOUBT IF THIS IS NOT ANOTHER SALARYGATE.