Zochitika za “End of Times”. Bamwani ma sachet kuti nzeru zanu zizitha komanso mmuzitupa. Bakhwewani ganjayo tidzakuperekezani ku Zomba muzikacheza ndi Bengo.
THERE’ S NEED TO STRENGTHEN IN THE COUNTRY NOT WHAT IS TALKED ABOUT SACHETS.
Venture Thupa
9 years ago
Aphunzitsi, nkhani yabwino, koma as you pointed out earlier that those are real sources of income to some disadvantaged parents for their children to b paid xool fees,if u ban these substances,still some pupils arenot going to make future anyway! In my case, I would suggest that all xools should always ban the use of these substances…& @ home parents should b responsible for their children to make sure they teach them the consequences of the use of these products. I don’t think the production of sachets should be banned as it is part of job creation in our coutry!
special advisor
9 years ago
Tax the stuff. Make it expensive to produce. Tax it. Make it unaffordable to buy. Ask that it be packaged in 5 and 20 litter containers. Make it difficult for kits to afford from bus fare money. Provide an alternative to young people. What is the substitute or alternative to alcohol. Youth want fun, excitement, …. What alternatives are there? What social structures and services are there? What about parenting? Many parents, especially, fathers all they know if to make babies. But they don’t take responsibility for nurturing them. In turn their son end up making babies that they don’t… Read more »
Concerned citizen
9 years ago
kodi anthu amene amamwa ma satchet asiya kumwa mowa ndipo kuti pano akuthamangira kuzintchito zawo zosiyanasiyana mam’mawa kukacha?
@ RICH
DZOONADI MBALE , MAYI AKO ALI NDI UFULU WOGULITSA KUMATAKO KWAO AS LONG AS SHE GETS MONEY
apao
9 years ago
Nde chambacho chimenecho, how come mukusiya kulesa mowa in general mukunena za chamba, ndipo sanena kuti chamba uneed civic education on this issue, ndi tsamba not chamba, osalesa mowa omwe mudaupangira lamulo la ddd i.e don’t drink and drive, uzungucracy basi, sungaone wekkha kuti amakwanisa to bring bread on his table nkumanganso nyumba yoposa ya a mp, mbuzicracy plus zungucracy, ur suporting whiteman industries osati black man’s. Mudazolowela kusungisidwa ndalama polima chimanga kenako kukagulisa mosikamtenngo komano kuti inu mukagule fertilizer koma kugulisa zokolola zonse kukagulako thumba limodzi basi, osalesa anthu kugula fertiliza bwa chifukwa sapindula naye, tsamba ndilodalisika man, asanena… Read more »
Zochitika za “End of Times”. Bamwani ma sachet kuti nzeru zanu zizitha komanso mmuzitupa. Bakhwewani ganjayo tidzakuperekezani ku Zomba muzikacheza ndi Bengo.
jada amwebwe pamenepa
Za zii ife tikanamwa pano tikulowela ku Jada basi
THERE’ S NEED TO STRENGTHEN IN THE COUNTRY NOT WHAT IS TALKED ABOUT SACHETS.
Aphunzitsi, nkhani yabwino, koma as you pointed out earlier that those are real sources of income to some disadvantaged parents for their children to b paid xool fees,if u ban these substances,still some pupils arenot going to make future anyway! In my case, I would suggest that all xools should always ban the use of these substances…& @ home parents should b responsible for their children to make sure they teach them the consequences of the use of these products. I don’t think the production of sachets should be banned as it is part of job creation in our coutry!
Tax the stuff. Make it expensive to produce. Tax it. Make it unaffordable to buy. Ask that it be packaged in 5 and 20 litter containers. Make it difficult for kits to afford from bus fare money. Provide an alternative to young people. What is the substitute or alternative to alcohol. Youth want fun, excitement, …. What alternatives are there? What social structures and services are there? What about parenting? Many parents, especially, fathers all they know if to make babies. But they don’t take responsibility for nurturing them. In turn their son end up making babies that they don’t… Read more »
kodi anthu amene amamwa ma satchet asiya kumwa mowa ndipo kuti pano akuthamangira kuzintchito zawo zosiyanasiyana mam’mawa kukacha?
ife nde wu not stop selling pano we have just designed plastic bottles instead of suchets but its gona b the very same price
amagailidwa ma sachetiwo?? amatola??? ndi ndalama amalipira ngati mmene umagulira sugar…alekeni akhale ndi ufulu wopeza anythn as long as u hv money