Email a copy of '‘Looterpol’ accuses State of using him: Malawi chief cashgater bitter' to a friend
Loading ...
Email a copy of '‘Looterpol’ accuses State of using him: Malawi chief cashgater bitter' to a friend
Malawi Congress Party (MCP) lawmaker Felix Jumbe has said he is being deemed as party “dissident”, saying despite rank and...
Seriously my gray matter is unable to swallow this. Lutepo remember u havn’t been stable from the begining, over-changing of statements. Anyway, c u afta 11 years.
Kutereku Unkaona Ngati Ukatchula Za Joyce Boma Likutaya Kumalimbana Ndi Joyce.Iwe Nkhuku Eti.Boma La Dpp Tu Lilibe Naye Ntchito Amene Uja Akamangidwa Amangidwila Zake Osati Kuti Bola Likumulonda.Ma Style Anu Athumbusuka Lero Tiyeni Zitchulanani.Nanu A Joyce Mutengerepo Phunziro Vuto Locheza Ndi Ana Amakutola Uchitsiru Chonchi.
Akuba okhaokha kupititsana ku ndende.
Ma judge athu, kuweruza mwachindunji. Tiyeni nawo osawasiya ayi, ankayesa ndi masewera.
Why did you accept to be used. Were you the only person within. Anthu ena kunalibe okuti akanawagwilitsa ntchito imeneyo if iweyo umawakonda nthawi imeneyo a Malawi. Munthu wophunzila ngati iwe sukanalola tha!!! half. Umadziwa kuti ukuvutitsa miyoyo yosalakhwa lero a Mbuye ayankha ndi la foti ili. Chowuluka chili chonse chidzatera iwe lero watera basi. Paja a Malawi timamva nkhwangwa ili pa mutu. Tiyeni nazo.
Uyu angolongolayu just keep him under lock and key. By the way I thought I heard that Mikuyu Prison was closed? Why send him there at all? Mukufuna muzimupatsa preferential treatment without any prying eyes. Why not incarcerate him at Zomba maximum prison or even Penu Prison in Nsanje?
The guy failed to play his cards well hence sticking to his “amandiyuza” syndrome & now he still tries to buy sympathy from the very same malawians he took advantage of. Mr Lutepo, I dont blame u, I dont even blame those whom u formed the looting team with neither do I blame the judicial system…..I just blame the BLAME itself for its existence. Hop its time to dance to the tune of your own music. How I wish i could see others of your calibar following u.
Lutepo. Where is this ape from? District?
This idiot is not showing any remorse
Za 92billion iwalani ndipo zisiyeni coz kunalibe this casgate.zikanakhala zoonadi nthawi imene kunatuluka nkhani imeneyi bwenzi JB atawamanga onse a app nkuwaponya mndende,tisaiwalenso kuti paja inali nthawi ya campaign.JB anangofuna kuipisa mbiri ya anzake poti yake inali itada kale.a Malawi anzanga cashgate ya 92billion njaboza kulibe sinachitike kafunseni a Reserve Bank akakuuzani ndanenazi.