Email a copy of 'Lucius Banda says UDF swallowed up, plot to unseat Atupele – Malawi press' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

47 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Angoni apa Phata
Angoni apa Phata
8 years ago

Bwana CHAIR handpicked Bingu. Bingu dumped CHAIR FROM UDF to form DPP . Now UDF wants to be under the umbrella of their rebels……… what adesperation by the so called ungonoungono.Soldier takauza a CHAIR…. sizabwinotu izi ife chipani timachikonda komano tikugulitsidwa.

Aufi
Aufi
8 years ago

Atupele ndi ka baby zoona. He has proved his political inmaturity

Raphael
Raphael
8 years ago

Tawawonetsani njira anthuwa a soldier anthu adyera awa anayamba akapangitsa sonkhano m’makwawo momwe adawasankha kapena angodzipangira?Eeeeeeeee!

Ingwenyama.
Ingwenyama.
8 years ago

My friend Lucius Banda remember what Peter’s brother Bingu did unto you in his power, takecare you will as well kiss the hot soup. And your UDF will be swallowed as you have said. Or its a plan that if Peter die Atupele will carry both UDF & DPP. Shame on the Yao and Lomwe Ignorant people.

Changaputwa
8 years ago

Wamisala anayiona nkhondo, pomwe alunga lungawo akadali comweco. Anthu amakutengani ngt ndinu openga kapena kt osokoneza pomwe mukuziwa comwe tinakusankhilani. Ngankhale nyakwawa samaweluza yenkha milandu popanda nthumwi zake kuunika, Onabo Tupele Msasu Muluzi akuyenela kubvomeleza kulakwa kwawo. Ngt osazitenga bwino palitu nyambo pansipo, cilipo comwe Peter yo akukonza ndicolinga coti anthese UDF. Anthu amatidwa ndi cimtuwisa kuiwala mabvuto ammadera mwawo.

Babalu
8 years ago

Kutha Ukuona.Pity

,MYEGHA,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,
,MYEGHA,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,
8 years ago

Tsopano akuti ino a Muluzi ndi JB munaloza Bingu. Kondi mukakhalatso kumbali ya boma? A DPP a ziwa kuti chipana cha UDF ntchofoka.KAYA ife anthu anu mukatiyika kuti? Tonse tipanga chipani china ngati sitipita ku PP

Stanley
Stanley
8 years ago

Plz soldier don’t follow this kid he is there to enrich himself come 2019

KUKHALA
KUKHALA
8 years ago

THUS WHY FAMILY PARTIES AR NOT GOOD FOR ANY DEMOCRATIC COUNTRY. LOOK AT OUR MOTHER COUNTRY’S PARTIES GOOD DEMOCRACY AT WORK. POLITICAL LEADERS WHOSE PARTIES FAIRED WORSE RESIGNED TO GIVE LEADERSHIP POSTS TO OTHER OR ALTERNATIVE NEW LEADERS TO ENHANCE PARTIES CHANCES OF PERFOMING WELL. THIS IS NOT POSSIBLE FOR MOST PARTIES IN MALAWI BUT FOR MCP. THEREFORE OWNERS OF THE PARTY LIKE A MULUZI WOULD RATHER KILL THIER FAMILY AT ALL COSTS.

Daphael banda
8 years ago

Dpp woyeeeee

Read previous post:
MPs calls MSB sale ‘most heinous corruption scandal’ in Malawi: Govt wants bank handed to Mutharika’s crony

Malawi Congress Party lawmaker Peter Dimba picked the controversial recapitalisation of state-owned Malawi Savings Bank (MSB) to parliament and described...

Close