Email a copy of 'Madonna bares boobs: Malawi goodwill ambassador ‘living for love’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Madonna bares boobs: Malawi goodwill ambassador ‘living for love’' to a friend
Consumers rights activist, John Kapito has lambasted Member of Parliament for Blantyre City South, Allan Ngumuya for defending Blantyre Water...
Shameful. Shes also known to use drugs.
Beyond signs of end times, what morals are we teaching de young…..
Even if she showed her cunt !!!!!So what! Lomwe girls and women do that in front of a whole Malawi President Peter Mutharika to an extent that ada chizeleza Vuwa Kaunda joins and dances with the boobacios girls!!Lo!
Mulungu akafuna kuchotsa maphumziro mwa anthu amayamba kaye kugwetsa onse amzeru mmzikomo.kenako anthu ndiye amasowa oti awasogoleri, ndiye amachitenga chimbuli chosochera mkuchipatsa ufumu.ndiye chimasochera mkusocheretsanso anthu onse.uyu APM mulungu samamudziwa uyu koma kachatsu basi.asocheretsa mtundu wa a Malawi.
Mmmm!!!
The picture was taken of 1st December 2014 – (Google Search: Madonna Photos 1 December 2014).
Our Malawi- Our People- Our Ambassador. But do we really know the definition of Ambassador??? This is pathetic indeed
Umbuli wa Amalawi tikulola satanic azimasuka kulimbikitsa uchimo.. Malo moti tilore atumiki a Yehova abweletse madalitso koma tifere ndalama za tembelero.. Umbuli mpaka apresident omwe kulora zopusa
Zimatakozo chimbinacho kukhwasula basi .
Alomwe timaonetsanso zimenezi Boobswill ambassador tsopano ommwe zamunyAnsa angoyamwa basi
mukudandaula ndi mabere a Madonna koma simukudandaula ndi Cashgate ya Mutharika ndi Joyce Banda atsogoleri omwe apangitsa kuti tizivutika. Opemphera abodza. Bwanji muchite zionetsero chifukwa cha cashgate? Kodi ku Malawi amai athu saonetsa mabere poyamwitsa?
JB ndi Mutharika anaba ndalama, tonse tiri chete. Koma Madonna waonetsa mabere, ndiye ikhale nkhani. AMalawi tiyeni tinene mavuto athu osati za Madonna. Ngati mabere a Madonna akukunyatsani ndi bwino musawayang’ane. You’re not God to judge Madonna.