Email a copy of 'Madonna give US$1 mil to her Raising Malawi charity' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Madonna give US$1 mil to her Raising Malawi charity' to a friend
Musician-cum-politician Lucius Banda on Sunday received rare praise during a Catholic homily in Mangochi for abruptly ending his musical show...
Thanks you Madonna for helping Malawians God bless you
ZABEDWA KALE.KKKKKKKKKK MALAWI WA MBAVA ZOPHUNZIRA.
Madona this madona that look how handsome the boy is now. Atleast his father can afford to board a plane now.
raising malawi ilipo? ili kuti? imapanga chani? yapangako chani pakatipa? yapangila kuti? important questions that neen answers.
anyway, can you send david home to mchinji for a while? nthawi ndi ino yokuti anthu amudziwe. aphunzile kunyenga pa andrews motel, kulima fodya, kugwira mbewa, gule….tikufuna adzakhale MP wathu kuno kenako ujeni wathu. mwana wa millionaire alibe nthawi yokuba ma change a amphawi akuno. zigawenga zinazi siziwona nkhope zikamapakula donor money.