Email a copy of 'Madonna plans to build more schools in Malawi ' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

66 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Grant C
Grant C
9 years ago

Pls madona,never change ure mind,continue helping us we realy need help to the pipo lik u

Chilungamo Chimawawa
Chilungamo Chimawawa
9 years ago

She teach girl children how to show off their boobs

aheli moto
aheli moto
9 years ago

bravo madona keep helping us

kanthu nkanko
9 years ago

Tiyenera kudzidalira pa ife tokha,mavuto athu ndionena kuti amene ali ndi ndrama ku malawi safuna kuti aziyendetsa ma company.mmalo mwake ma company akutsogoleredwa ndi akunja,chief director manager wakunja,gernaral manager wakunja.Exactive manager wakunja,financial manager wakunja,chief engeenia wakunja,akumalawi pa secretary,asistance field manager, washman,stores keeper,mmalo mwake akunja akutumiza ndrama zao kunja.kodi anthu akumalawi alibe ndrama kuti azikhala ndi maudindo mma company?nanga sanaphunzire?pitani ku Tanzania Boma lawo limapangana ndi onse obwera ndi ma company kuti udindo waukulu uzikhala ndi eni company koma wachiwiri uzikhala ndi waku Tanizaia.ife ngati si tisintha tizipempha kwa madanna mpaka chimaliziro cha malawi.anthu azititengera ana kuwapitisa kumene sitikudziwako kuti pa… Read more »

Paul
9 years ago
Reply to  kanthu nkanko

@Kanthunkako is it about Madona or muli ndi vuto lina lofuna thandizo. Coz wat U r saying is queit contrally ndi za Madona.kkkkkkkkk funny indeed.

robert likangala
9 years ago

Kodi madonna yo mukudziwa zimene akuchita ndi anawo kusere konena kuti akuwa phunzitsa xool?koma umphawi ndi matenda,osauka alibe chisankhu makamaka ngati alibe Yesu.Aliyense ndifumu kwa osauka,kwa munthu osauka osaukanso Yesu,amalandila chilichotse,amatengedwa kulikonse,amalandila thandizo lililonse,amamveranso chilichonse.pamwamba poti madanna akuthandiza koma malawi achenjere si zaulere pansi pali dipo limene malawi apereke kwa madonna,izi zitengela amene ali ndi ditso la uzimu kudziwa.

Okonda zinthu
Okonda zinthu
9 years ago

Naye mese james akungooneka ngati ali kumalawi konkuno. Anthu omuona aziti amaphunzira pa chisamba LEA. Aaaaa alimbuu kamphunoko apite naye ku surgery. komanso uyu David aaa kungokhala ngati sanasambe bwino bwino… AAAA atamawapaka polish anawa. apo bi angowagulira shine bright Vaseline azikaoneka bwino..

Hoitty
Hoitty
9 years ago

Mercy James mwana osamva nyengo za snow ndi stock margarine. Tsopano a Madonna kuzikutira choncho pagulu la anawo kutentha kumeneku chikhale chani? Kuopa ma germs?

Peter Mathanyula Wakuba
Peter Mathanyula Wakuba
9 years ago
Reply to  Hoitty

Hahahahahahahahah. Lol. I made the same observations as you (both on mercy James and on madonnas dress). Lmfao. You took the words right out of my mouth Hoitty

Koma
Koma
9 years ago

Tsopano david, osapesa tsitsi ngati bambo ako choncho? Anga uli kudambwe, tapangani za chi black american please!

pitala mulakho
9 years ago

TAMUUZANI MADONAYO WATSAMIRA MWANA AKULIRA KUMBUYOKO INDE NDIFE OVUTIKA KOMABE APOPO WAWONJEZA

Atujumile Oponyo Ritchie
Atujumile Oponyo Ritchie
9 years ago

She withdrew her money after being suspicious of my embezzlement of funds from her initial project when she wanted to construct a girl’s school in Lumbadzi. I was then apointed PS number 4 at the Ministry of Education by my sister JB, of course that was out of my expertise not nepotism. But I told my sister that Madonna should nit step a foot again in Malawi. I and my colleagies at Raising Malawi unsuccessfully attempted to sue Madonna for firing us. Anways she can go ahead, its DPPs time andI wish her all the best. She has the last… Read more »

Read previous post:
Lilongwe Mayor faces crisis of confidence from councillors

A group of councillors are working on plans to unseat Lilongwe City Mayor WillieChapondera. According to information sourced from Lilongwe...

Close