Email a copy of 'Madonna posts  Malawi twins photos on Instagram to confirm adoption: 'Happy’ girls flown to New York' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
FreeTechAdvise
FreeTechAdvise
7 years ago

This lady has a heart.

chindindi Joseph
chindindi Joseph
7 years ago

zilibwino

trevor kasakatila
trevor kasakatila
7 years ago

Koma mzungu uyu ndi wabwino kwabasi!!!!

Bravo Madonna
Bravo Madonna
7 years ago

Nyani wina akwiya ndi nkhani imeneyi. Azikamba za Yesu. Lol. Yesu wakoyo bwanji samaapanga adopt anawa?

hehede ine kusekelera
hehede ine kusekelera
7 years ago

Mwana wa chimalawi. Sangaiwale toy yake ngakhale akupita kwao kwa mzungu. Ndodo yake basi osaitaya cholinga azikwerapo ati njinga kkkkkkkk. Zosangalatsa kwabasi. Muyende bwino ana anga Mulungu akudalitseni. Mukukalowa ku Disney World likulu la ma real toys osati zingelengele kapena kumakwera pa sache kapena saka lakutha kumakokana ati wakwera galimoto iiiii!!! Mukamazabwera osaiwala kuwatengera asuwani anu mwawasiya aja timakabudula takutha. Zikomo

Mika Kumbire
Mika Kumbire
7 years ago

Wangokula ndi umphawi bwana. Some of us pay school fees for the neady children and orphans in Primary, sec school and college. And as you may appreciate, we do not support these people out of abundance but through sacrifice and care. Assistance takes different forms and levels. In the West there is no extended family and support and dependence stops at age 18 on the dot.

Koma kwathu kuno anthu kusakulanso. You may for someone’s entire education; you may for their lobola and chiongo, you fund their chinkhoswe; kenako chikwati. You pay for maternity medical bills. Mwana wobadwayo umulipilirenso school.

The Analyst
The Analyst
7 years ago

O…………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………….O “In the middle of difficulty, lies an opportunity.” – Albert Einstein. Kodi inu . . . . . . Who is kept at an orphanage, if not kids who have had their parents die or suffer absolute impoverishment? And wherefrom, was David (and the others) adopted (by Madona) if not at that place where only abandoned kids are found? . . . Kodi inu, what’s the probability that these kids will die poor under the wings of a parent with an estimated net worth of US$560 million? . . . Yes, money is not synonymous with happiness, but who… Read more »

Zoona zake
Zoona zake
7 years ago

Better USA orphanage than Mchinji orphanage. Well done Madonna! Wakwiya ndi mfiti! Nanga mmene ulili umphawi pa Malawi pano wina mkumakaniza ana? Bwanji ngati mumawafuna simuwathandiza pamene anali pa mabvuto? Kodi bwanji mumasangalala anzanu akamabvutika? I wish slave trade ikanabwerera kuti mwina atigule ife tipite kunjako! Kuli bwino kukabvutika kunja kusiyana ndi umphawi wathuwu!

Chilombo
Chilombo
7 years ago

Damn!!!! What a way to enter the U.S. I’ve never been even on a commercial plane and these twins first flight had to be a private G-4? Wishing you all the best as you start the life most of us will never have.

Read previous post:
Justice Mwaungulu laments error-riddled appeal documents on Chaponda: To rule on Friday

Justice Dunstan Mwaungulu of the Supreme Court of Appeal say he requires more time to study further the arguments raised...

Close