Email a copy of 'Madonna’s Malawi twins’ dad claims he didn’t realize adoption was permanent' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Madonna’s Malawi twins’ dad claims he didn’t realize adoption was permanent' to a friend
Controversial mang'anja chief, Paramount Lundu of Chikwawa on Saturday surprised people when he refused to sit next to fellow traditional leaders...
Shut up! u good 4 nothing man, very irresponsible, very unloving and very inconsiderate. Forget about d kids
kupusa kumeneku ndiye muziti Ochewa adzalamulira ziko Kkkkk kapena Ochewa 2019 Boma kumbwabwana kwake kumeneku? E ndavomera Ochewa ndi Boma Koma Boma Lake la Mchinji la omwale. Iwe Mwale ndiwedi zimwale waona kuti Fodya sukolora ndiye Ufuna ubere Madonna ndiye wagwa nayotu. Zoyakhula zake ngati mwanatu manyi ako ndithu.I think is whole central Region kuli wanthu Ambirimbiri ngopepera maganizo. Look how Bakili described Malewezi?. Ochewa ziko LA Malawi Sanalamulepo Sadzalamulapo, Kamuzu sanali chewa okuba wa ku Ghana uja, Anaziwa kuti abwere ku South akawayimbe mijomba saitha, or Alhomwe sakwanitsa, Asena samumvera or ku North atumbuka akanamuyngako kale kale ndipo amaona… Read more »
The gentleman is very stupid and silly. All along claimimng the kids after been adopted by a rich person yet didn’t give a hand in raising the kids to an extent that they were been assisted by charitable organisation yet he is still alive I see.something is not right in his head. Ok if Madonna says here are your kids what will happen ? Will he be able to keeps the kids.this.time. Man just keep quiet your job is only fucking not taking care of the kids so close your stupid mouth.I don’t mind if these kids won’t see you… Read more »
shaa koma mbwambwanest iyinso nde yee..eti kuchita kunena opanda manyazi kuti, they were going to a rich woman’s house to get proper education so that they can come back to ‘help’ us, really!
Akuluakulu, oMwalewa simukuwavetsa bwino. Iwotu chimene akudandaula ndi choti kodi adoption
angochita ana awo okhawo? Iwonso akufuna adoption??kkkkkk!
jst be grateful mr
Inu O’Mwale, aayamikani kuti enanso atola anawo momwe munawataila ku Orphanage’ko. Mukadakhala kuti mumawakonda asungwanawa, bwanji mutakwatira mkazi winayo simunakawatenge nkumakhala nawo pamodzi ndi mkazi watsopanoyo kuti alele asungwana anuwa?
Mr. Mwale, just be proud kuti you now have children who stay in USA basi…. Is it not better that the kids are now at someone’s home than an orphanage?.
HERE COMES WHAT WE KNOW ABOUT MALAWIANS
PRETENDING NOW TO TRY TO GET MONEY!.. WHO CARES WHAT HE THINKS. THE CHILDREN WERE AT
AN ORPHANAGE.. HE WAS ONLY A SPERM DONOR AND DID NOT TAKE CARE OF THEM
GO AWAY!.. GO BACK TO THE BUSH AND DRINK CHIBUKU
Best of them? Ku orphanage kumapezeka ma best?