Email a copy of 'Maintain current squad in CAF, Kondowe urges Bullets' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Maintain current squad in CAF, Kondowe urges Bullets' to a friend
Malawi former president and Founder of the Joyce Banda Foundation International, Joyce Banda, on Tuesday, December 9, 2014,held a high-level...
Tiyeni tipereke suport yokwana ku team ya bullets osayang’anira ku ma team omwe tikuchokera uwu ndi mwayi umodzi otukukulanso dziko lathu. Pempho langa kwa ma player a bullets ndi loti musamakhumudwe ma coach anu akamapeza ma player ena sikuti akukutayani, inuyo mpira mukuutha pitirizani.
Dats tru they nid 2 add player
Iye number 13 iwenso ndi kape weniweni. Apa Jahman sakukamba za nyerere apa ayi. Ukanene zanyerere, chomwe nyerere zikuwakhudzapo apa ndi chiyani? Iye akukamba za keeping the same players or beefing up squard of Bullets team as they are preparing for the CAF championship. Ukanene zanyerere waona anzako onse amane akomenta atchulapo za nyerere apa. Inunso ndi achitsiru bad.
Indeed we need to add force
sakunama koma tionjezere angapo chifukwa caf sizibwana
Fischer akunena zoona komabe CAF imafuna 30 players ndiye kuonjedzera anyamata angapo kufunika. One striker,a goalkeeper,two midfielders and two defenders will be fine.
but we need to source a lethal striker
60% is not much give. We know you have spent alot to finish league but for the administration sake give. That will boost the players for the next season. Even new players will get attracted.
BB NDI DIL
WHEN PREPARING FOR A BIG TONAMENT LIKE CAF YOU HAVE BEAF UP THE TEAM. THAT DOES NOT EGNORING THE OLD PRAYERS. CREATE A COMPITIVE SPIRIT.KONDOWE YOU ARE NOT WRONG BUT MIXT THEM OLD AND NEW.