Email a copy of 'Maize prices rise by 37% in Malawi -Admarc' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

35 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
johnkaitano
8 years ago

komabe nzeru za munthu zalephera kutetsa njala, kwa anzungu nawonso akulephera kukonzanso nyengo yowonongeka, pakibe ali ndi nzeru.

Critical thinker
Critical thinker
8 years ago

Malawians suffer because of poor choice of leaders.The yard stick for electing somebody is names,titles and tribalism.They don’t look for policies.So don’t cry of hunger.Pitala and his entourage are feasting on xxxl chicken and chips at Hilton hotels washing down with some expensive juices.Koma Ndiye mufotadi ndi njala kamtundu kopusa ndipo kosamva.Koma ndiye mukhauladi ndi mlomweyi mpakana 2019.

Alex Tulamah Tulamah
8 years ago

Tikapita ku joni akutiphako tikhale kwathu kuno mbeu dzikupysera m’munda nanga tipange chiyani ife anthu anu ambuye. Atsogolerinso zoti kulinjala sakusamala ai akuti bola iwo akukhuta. M’malo mugula chimanga akuononga ndalama kutengera anthu kuka nyada kunja votiyanga ija ineeeeeee!!. Ndinabetsa

Alex Tulamah Tulamah
8 years ago

Dziko langa lija ine talakwanso chiyani nanga kodi chalangochi chikufikira ifenso tikhululukireni YEHOVA, ndikudziwa masatanic ndi amene akupangitsa mcholinga choti anthu avomereze kuti anthu akhazikike pokwatirana okhaokha nchokinga akuti tililandila thandizo lo chokera kwa iwo oyipayo Mulungu wangatu akuona athanananu

baby
baby
8 years ago

I think Malawians are the most stupid people on this planet earth. It’s normal when supply is low, demand is high, price increases, simple. If we had bumper harvest as a nation, the price of a bag of maize would not have risen simple!!!

ben matemba/nakhule/chiradzulu

NDE TITANI PAMENEPA MOYA CHE MUTHARIKA PANGANIPO NGATI MAMUNA APA ZISANADEPO

mpimpa
mpimpa
8 years ago

kaya

wez
wez
8 years ago

Ife tidanena kuti awa mbuyache aabwelesanjala kumalawi kuno,sizimenezonanga…titoona kumenezitatheleko!

Sambaukwatiwe
Sambaukwatiwe
8 years ago

Its high time the Mw gvt should think of removing fertilizer subsidy, becoz we are losing out 50 billion Kwacha on fertizer subsidy but its not giving us the intended results unlike removing serving K22 million for JCE printing of certificates

prophet of dome
8 years ago

kkkkkkkk malawians too much crying. Nthawi munalinayo yokoza dziko, mumafuna chimanga 4. Lero mwaziona. Mulungu akulangeni kwambiri mufe ambiri ndi njala imene mwina muphunzira kusankha bwino. Tsogoleri akakhala wabwino dziko limakhala lamadalitso. Koma iri mavuto ngosayamba tilira.

Read previous post:
Malawi teen calls for international support on girl-child education at UN

A 13old Mtisunge Kamphale has pleaded with international organizations attending the 70th United Nations General Assembly in New York, United...

Close