Email a copy of 'Makande arrested in Malawi ‘cashgate’: Turns himself to ACB' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

47 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Domi Phambana
Domi Phambana
9 years ago

apanidwe mpaka abweze zonse,amine kuti mfiiiiii!

Alex Matinga
9 years ago

Wawa Bammbo Makande!! Lyo!Lyoo!lyoooooo! PP woyeee! Mwana weniweni wa mayi chiongolelo ameneyu. WATCH OUT GWENGWE!!

Think Tank
Think Tank
9 years ago

@ Blues,let us not be carried away with our imaginations. German has given almost 10billion kwacha to audit 2009-12 period when these audit querries arise. Germans are not fools to play silly games and throw about monies. Pati biii pali munga. Those of 13billion are facing it now. The 92b culprits wish time stands still to avoid their destined fate.

DR. SAN- ABACHA . WAKUMALOWA -KWAMAGODI
DR. SAN- ABACHA . WAKUMALOWA -KWAMAGODI
9 years ago

Ogonakukhomo kosatseka akulumidwa ,udzudzu kundende kikikikikiki ine ndiri mu net yanga ndi akazanga pheee ,

wa ku Mitchesi kuja
wa ku Mitchesi kuja
9 years ago

Inu ACB, musamaulule m’mene mukuchitila ma “investigation” ai. Kwenikweni za JB. Musapuse nazo; mwina akamva, sazabwela. We want her in Zomba Maximum!

Lephert
9 years ago

Ndale zakumalawi zimenezo….DPP ikadzachokanso nkhani za cashgate zidzakhalaponso

Dodolido
Dodolido
9 years ago

Mukunama , Makande? Makande wake uti? Bodza lankunkhuniza. Nda amuna amenewa ogona kukhomo kosatseka, sangamangidwe.

Mapwiya Mng'onong'ono
Mapwiya Mng'onong'ono
9 years ago
Reply to  Dodolido

ndiye mwati Makande ndi mamuna sangamangidwe? Ngati muli ndi makutu mwina by now mwamva

Phwetembwe
Phwetembwe
9 years ago

Put cashgaters in a cooler without mercy but next be 92 billion cashgaters dead or alive. All must face justice & make sure they return all the cash to government. Malawians be careful the returned cashgate money can be cashgated by DPP since our focus is only on PP. Mark my words!

chatonda
chatonda
9 years ago

Tiye nayoni anasimbwa agalu amenewa. By the way, where is JB THIS TIME ROUND? HAS SHE COME BACK FROM WHERE SHE WENT TO BEG AFTER THE CASH GATE STOPPED?

sifiso gebuza
sifiso gebuza
9 years ago

a makande ndiye sizimakuthelani, chaposachedwapa munamangidwanso pa milandu ija ya ‘kangwazi’ ndi mbaza zomwezi za chilomwezi pano ndiye zikukakamirani koopsya mukathera konko basi!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

Read previous post:
Malawi aid debate in UK House of Lords

The House of Lords in Britain will debate a Motion on aid to Malawi on Thursday, Nyasa Times learnt in...

Close