Email a copy of 'Malawi army ready to deal with peace breakers – General Supuni' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi army ready to deal with peace breakers – General Supuni' to a friend
Malawi Congress Party (MCP)president and leader of opposition Lazarus Chakwera see sense in the suggestion by civil society organisations (CSOs)...
Mr. Spoon, I hope you revisited your speech and saw how stupidly and cowardly you sounded in front of your soldiers and their wives and children.. Army yotani yoopyeza anthu ake mmalo monena zoteteza malire a dziko lake.
Shurrrap u Supuni! This army has never ever fought a war- it only fights in beer halls and with mahule! Useless army of mbava and diseased fornicators. May u rot in hell with ur dunderhead Mutharika!
GENERAL FOLOKO !!!
BE REMINDED THAT KWASALA ONE AND HALF YEARS BEFORE YOU ARE FIRED .ANTHU AMENE MUKWAOPEDZA SADZAKUSIYANI BWANA . OHO INE NDANENA NDANENA
mmalo mokateteza nyanja uko tizilimbana tokhatokha zoona
Buying vehicles because of the accident ,does it mean you were not aware that your troops were not using proper armored personnel carrier..You must be a twatt or sloppy Joe sleeping with a rifle pointing on his foot..Munaphetsa ana aweni because you just don’t care about their welfare…Mwanamizana ndi Peter the dodo,remember you have relatives outside the barrack’s and on facebook..These uwone
Supuni Munthu wakuba,thats not your job ,mwayamba kulowelera zaweni..bwanji mukalande Nyanja ija anakulandani makape inu…You should not even poke your greedy nose in politics if you are a professional soldier,koma paja inu ndi mbava.Tayesa uwone mwina umayenda m’mbali stupid post deserters,kuthawa Ku congo kusiya mfuti mbuyo mwayesa Suriname,cowards
Akufuna azitetezana akuba wokhawokha. Chirichose chiri ndimapeto ake. Lucius anayimba kale kuti anthu aMulungu sangakhalire kuvutika moyo wawo wonse. Zivute zitani opanda wowadalira mulungu azawapatsa zofuna zawo.
Amene amathothola amakhala amaudindo aang’onoang’ono. Akuluakulu onse asanduka mbava ku Barracks za Malawi.
Pitala wakunamizani a Galu inu mukufuna muyambe kuzuza anthu koma mukuyidziwa ntchito yanu ? mmmmm musalowelele za ndale …….tiyene tithandizane kukankhila kwa kuya bomali lichoke latinyasa kwambiri.
Work within your mandate otherwise we Malawians are not going to accept nonsense