Email a copy of 'Malawi army soldiers kill 2 over Dzalanyama' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi army soldiers kill 2 over Dzalanyama' to a friend
Malawi police in Blantyre have launched a special operation to hunt down murderers that have killed some people in the...
Ntchito Ya Asilikali Ndi Imeneyo. Palibe Chodabwitsa Apa.Ngati Mukufuna Mtendere Itanani Apolisi Asilikali Achoke. Failing Which Anthu Apitirira Kuphedwa Ma Soldier Samachita Chibwana.
Zodiac broadcasting station is a stupid radio station that i have now stopped listening to now. No moral responsibility whatsoever. You know they put this story as its weekend feature story! For what! Nyasatumes.don’t join stupid zbs
Comment 40, 12 and 6 i agree with you guys, the army are not above the law afterall iwowo akalanda makalawo kapena mitengoyo what do they do with them . A kansala take the matter up, find out why mitengo yachilengedwe yodula koopsa imene analanda a MDF yasowa ku MDF heaquarters komweko after Commander wolamulira asilikali olanda makala, mitengo ndi kupha anthu atalamula kuti mitengo isamalondeledwe cholinga choti abe akagulitse for millions of money. A president chonde pakhale commission of inquiry into the death of these two. the other thing is we wonder why now these soldiers are killing civilians… Read more »
MALAWI FEEL SORRY FOR YOURSELF LOOSING A LIFE IS NT A JOKE
Akuchita bwino a army kuteteza nkhalango ndipo amakala awa amakhala ndi zida zoopsa ndipo izi ndi zina zomwe zimawonjezera mkhwiyo mwa army athu.
Long Live Malawi Defence Force, Long Live Malawi.
Killing defenceless people. Is this the sign of might on the so called MDF? Imagine killing an 80 old granny. Do we really have sensible soldiers that a country can be proud of? Whoever is applauding the behaviour of these useless so called soldiers should be ashamed of his/herself.
Zoona zake ndizoti Boma lipeze njira yoti aliyetse wa kumudzi olo wamtauni asamaphikire makala basi. Nchenjezo ndiloti army ngati mukuphadi anthuwo siyani chifukwa Mulungu sakondwera ndizophana ayi. ngati mwaphadi pemphani chikhululukiro kwa mulungu akukhululukireni basi. ziwani kuti umphawi ndiumene kukupangitsa zonsezi kuti anthu aziwotcha makala kuti apeze chakudya chalero.
pathako panu amene mukuti a Army KUCHITA BWINO MCHITIDWEU…..Once again pankholo panu….. kuchokera pa Kampepuza, Msipe, Balaka market, Chingeni, Manjawira, Senzani, Chitale, Phalula, Kanono, Kamwamba kuzafika Zalewa malo onsewa munali nkhalango koma mitengo anamliza…..mwano wake nkumachita kuyala makala mbali mwa nseu. bwanj ngati muli oteteza osabwera malo amenewa kuzapha anthuwa? Ndakwiya nanu
MUKAONE THUMA FOREST ANAMALIZA KUMENEKU MUPITENSO ARMY
If that is true God is watching u repent ur sins