Email a copy of 'Malawi Cabinet reshuffle brings great expectations: Mutharika to rejig his ministerial team ' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Cabinet reshuffle brings great expectations: Mutharika to rejig his ministerial team ' to a friend
Malawi Congress Party (MCP) president Lazarus Chakwera has been touted as a man to deliver Malawi from the rogue nation...
Za ziii ati kuonjezera maunduna kuti adzawinenso. Anthu ovota ali ku mudzi osati mu cabinet ayi. Zopusa anthu ene kumasangala ndi zozizira ngati izi. Uladi Mussa walowa dpp kuti mulandu wake wa ma passport amuphimbire. So when Chakwera says Pitala is the prince of thieves, lomwes say Chakwera is jealousy. Tionana 2019. Kumwerako kuli wathu Sidic Mia ngati mukudzinamiza nafenso tipezako mavoti kumeneko.
So Peter Mutharika can change regional committees anyhow, but when it is Chakwera people cry foul! Okay.
Boma ilo! DPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPPP
Brother Maunitsi zinyadani ndi munthu wanuyo. The highest he can achieve ndi u Leader of opposition. Satan is the one who opposes God. Here on earth satan is the one who opposes government. All the best maunitsi ndi satana wanuyo.
Ndava chisoni koopsa!! Ee koma man apa mwalankhulatu wawa.
Jooma I believe would make a good addition to Cabinet, Uladi I am not so keen he is just a tidye nawo but if he can bring in votes ok let’s give him another chance but he has too many scandles. I guess In this reshuffle the president is trying to balance government performance and Political mileage. That’s tough gaining Political mileage could undermine performance but if done right he can get the performance going and that could drive his ratings up. I believe his main concern is votes so I won’t be surprised to see the old boys back… Read more »
Kodi tikadzawinanso aMalawi onse adzasangalala osati Mulakho okhaokha?Paja pakalowa njokatu chenjera Kandodo.
ONJEZELANI MAUNDUNA BWANA KUTI CHAKWELA APHYE MTIMA KKKKKKKKK 2019 #DPP BOMAAA!!!!
Suzungwilizana ……kupusa ndiye kumeneko!
A Chilenga akatanimo mu cabinet. Awo ndiye masewara apanchenga tu tsopano pitala.
kkkkkkkk koma kumeneko njenje njenje a Chakwera mwawawona eeeeeeeee! Ife tili nyodoooooo! ndi Chakwera wathu.
When you do something good, you are always shouted by PAC. The best way is to do bad by increasing cabinet to 26 so that PAC`s shout should be genuine. Ngati madam kunyumba nthawi zonse amangoti amunanga zibwenzi pamene zili zabodza, pedza chibwenzicho kuti akamakunena zizikhala zowona.