Email a copy of 'Malawi Catholic priest jailed 17 years for sex abuse on girl, 15' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

24 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Amos
5 years ago

Eeee koma iwe amene ukuzitchula kuti MAPWIYA anakupasa pakamwa. Ukuyankhula ngati ndiwe mnjelo bwanji. Kulitu ansembe abwino dedicated to their calling and serving the people of God. Ndiye kuti iwe basi ukangowona wansembe aliyense wamuweruza kale? Iwe ndi mulungu? Your comments sucks. Galu

Mutumwa
Mutumwa
5 years ago
Reply to  Amos

Wanena zoona mapwiya akulu! Vuto lake ndilimenelo, mumadana ndi chilungamo kuti mudzioneka oyera, pamene ndi inu ziwanda zokhazokha!!!

cham'madzi
cham'madzi
5 years ago

Mwanayu ndiwabodza lankunkhuniza. Iye amalolera bwanji kumupangira rent ku Liwonde, Balaka , Lilongwe mpaka ku Zomba? Izi zidali zogwirizana. Makolowo angofuna kuwapanga chipongwe abusa. Komaso abusa mwatichititsa manyazi ndi khalidwe lanu lonyasalo.

Ndaonavino
Ndaonavino
5 years ago

Too bad but the fact remains that the lady was once married and run away from the first marriage because of the father. The question to be asked is between the father and the husband who was supposed to be jailed?

Gerald Mapanga Phiri
Gerald Mapanga Phiri
5 years ago

Where are these people always commenting bad about Prophetic ministries? Come out

Shaka
Shaka
5 years ago

Gerald, they make such comments out of ignorance. Those of us in the Prophetic ministry know the truth. Make no mistake this case is embarrassing even to us in the prophetic. Vuto lopita ku ensembe as a form of employment and not a calling. Wina ndi uja Ali ku ndende because of an issue to do with killing a person with albinism.
Am not happy with the lenient sentence he has gotten.

AGUNDU
5 years ago

Aaaaa Sembe ngakhare ndinu anthu ngati tonse koma mukutichitisa manyazi kwambiri. The church is in disrepute because of your behaviour. Just resign and mukakwatire. last 40 ndilimenero?

Mkaika
Mkaika
5 years ago

Wansembe ameneyu ndekuti masamu amamuvuta eti kulephera kuchotsera 2018-2001=17. Kunangotsa chaka chimodzi kuti kuti kadona kakeko kapatsidwe Sex Certificate.
Komatu azinzanga pano tidziwe ichi ansembe saletsedwa sex amaletsedwa kukwatira. Nzithu ziwiri zosiyana.

Mapwiya
Mapwiya
5 years ago

Mpingo wa Katolika uhule too much.?Mowa ndiye sinkhani. Ansembe kunamizira kuvala zoyera mkati muli mimbulu kunyenga akazi a eni ake kupha ma alubino kunyenga ma sisitere. I said already kuti Catholic si mpingo ai koma chilombo chotuluka munyanja .Read Revelation 7 and 12. I am very happy with this lengthy custodial sentence may be ena atengerapo lesson. Mpaka kumanena kuti mwanayo sanali mwana? Naye defense lawyer kumaimilira za utsiru ngati izi. Ansembe onse vulani mikanjo mukwatire basi osamamiza anthu

POLICE
POLICE
5 years ago
Reply to  Mapwiya

You have said it all…………….. i couldn’t have said it any better!

Guantanamo
Guantanamo
5 years ago

chilango chakula mpaka 17 yrs? anali armed robber?

Gule Wankulu
Gule Wankulu
5 years ago

The girl consented. She also lied about her age to the priest.

That wasn’t abuse. It was just a slip of the penis…….

Shaka
Shaka
5 years ago
Reply to  Gule Wankulu

Your name says it all.

mapuyamurupare
mapuyamurupare
5 years ago

I salute the magistrate. May God Bless you.
You are really Patriotic and honest.

Read previous post:
Chimulirenji visits fire victims at Lilongwe Teachers Training College

The  Democratic Progressive Party  (DPP) presidential running mate, Everton Chimulirenji, Thursday morning visited Lilongwe Teachers Training College (TTC) whose hostels...

Close