Email a copy of 'Malawi civil servants demand pay rises to match true cost of living: Warns of strike action' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi civil servants demand pay rises to match true cost of living: Warns of strike action' to a friend
Last week soldiers from all Malawi Defence Force (MDF) units gathered at Malawi Armed Forces College (Mafco) in Salima for...
childish government that changes policies any how,
Kodi financial year ikuyambira December kapena July? Chonde zibwana ayi.
zosekesa kwabasi ndipo sitilola zonyasazo.
Malipiro akuyenera kukwera pa 1 July 2015 ndipo zingavute maka tiwathandiza ma Junior Civil Servants kupanga zionetsero ikangophasa bajeti without proper wage bill adjustment and change of time frame from the abnormal December to normal July.
Zandudu
Why increment effective December while financial year starts this July.Ma civil servant mukanati mudziapatsa salary yabwino,mavuto aulova bwenzi ali ochepa chifukwa bwenzi nawo akulemba anzawo ntchito.Advice is like a second mother to a child.A boma konzani zinthu kuti mukhale bwino ndi a ntchito anu.Mapeto a zonse opindula ndi eni amalawi.
Goodall Tipe Waka Ndalama,sazacha
Petulo Mutharika ndi saulo chilima amati sakufuna kut anthu azilandira ma change.ndiye kupanga strike n’kwabwino chfukwa ayiwala zomwe analonjeza.
Ationjezele basi
Goodal Gondwe chimunthu cha nkhaza musaiwale anabweretsa policy ya three yrs pension lero akuti december chaka chamawa adzanena february 2017.
Tasintha boma koma Palibe chikusintha malipiro bola amayi omwe aja Tinamva kuti a Chilima akufuna akonze civil service kuti anthu azilandira ndalama zokwanira koma pano anasiya ndikumveka komwe. Mai ine