Email a copy of 'Malawi coach says mountain to climb, skipper upbeat in Algeria' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi coach says mountain to climb, skipper upbeat in Algeria' to a friend
Azam Tigers Technical adviser Robin Alufandika blamed the barren draw with Civo United on Sunday at Kamuzu Stadium to poor...
These coaches have had their time and should be rested if the team has to go forward. They continuosly misread the game and misposition players. Anyway they are ex – defenders faced by a team which does not score. They need to brief players in gaining composure and confidence when approaching the goal area.
Citizen
If I were the coach I would tell all the players to make a wall at the goal line so that the ball should fail to pass through. Automatically it would have been a 0-0 game. Try Kanyimbi to be the coach you will never lose.
Ndizoona kuti ayese kutenga ma strikers a super league komanso simplex Nthala akanatha kungomutenga kuti adzangoona kuti fitness yake ili bwanji chifukwa pagolonso
pali bvuto.komanso coach akamasintha ma players adzitha kuona kuti akuchotsa
moyenera, chiukepo sanadzuke bwino koma anayamba kuchotsa ngalande, kumusiya chiukepo.Apanso panatidabwitsa,ifenso masapota tiyenera kudzudzula mwaulemu
osati ,kungonyozaamzathu popanda chifukwa cheni-cheni.
Bambo anthuwa amalandira ndalama zathu. Osawanyengelera kodi azawina liti? nthawi zonse kumangoti tikukonza timu tikukonza timu mpaka liti?
zatikwana zomangoluzazo till when?kuti tidzakondwe
Mwachinyidwa amalawi ife muone tipange yathu team,bwenubwenu fc
3 Nil sounds fair… Coach out !!!
Chiukepo siwapira
I was thinking of bringing kinnah phiri back,kkkkkkkkk, kodi coach mzungu pano mmene ya sinthila ndalama ku soccer tingakwanitse?. Kinnah was the best and be treated as such,kodi team inkapanga ma draw ndekuti sinali bwino?,stupid regionalisim activits,….
Mumuuze chiukepo sizongomenya mpira chimenyemenye him as a striker he should try something when he reaches in the 18 yard box osati zamangolomelazo ayi
Even though we just take it as fulfilling the fixtures,this is the time guys with a lions heart can prove themselves.If they did it at the stadium why cant we did it at their backyard and show the world hahaha guys if you want jobs to play ion europe this is the arena to show that you are capable.
Palibe amwene abandulidwa kale dzulo 3 mwa ndanda kapena kuti mwa zero.