Email a copy of 'Malawi Congress Party downplays feuding talks' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

12 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Richard Pangani
8 years ago

Wopandaphindu ngatiuyo kumafunabe.

Pa zedi
Pa zedi
8 years ago

Gustav, munthu wokonda chigololo too much. Kukonda kanyenga akazi a eni. Don’t trust him. Pubwa wachabechabe. Onani masowo, in a MCP, amakunamizani chani big crookuyo.

Sibeko
Sibeko
8 years ago

Go go M.C.P 2019 bomaaaaaaaaaaaaaaaaaa! Peter, Joyce aaaaaa mabi eni eni makamaka chopanda mano mkamwachi chikutiluma amalawi

Masharubu
8 years ago

Njobvuyalema, we want you as our president in MCP. Who else is experienced and know better MCP politics than you? Atifunse ife kumene tachokera ndi chipanichi. Njobvuyalema go. We are behind you.

Lord Mansfield
Lord Mansfield
8 years ago

Kodi Anthu Enanu Muvutikilanji Mukamba Za Bisnowaty, Jumbe, Njobvu Pamene Chipani Chathu Chili Bwinobwino Sindinu Ma Member A MCP, A MCP Enieni Tikuziwa Kuti Zose Zili Bwino President Ndi Mmodzi Yekha Chakwela Basi Exctv Ili Bobo, Inu Zilimbanani Ndi Awa Akulephela Kuyendetsa Boma Pano Zpwilikiti Pa Poly Nanga Mavuto Osatha Ali Mmanyumba Mwanumu, Amayi Nde Angohangaikahangaika Kunja Kuno Udindo Wao Pali Vacancy Akakhala Atupele Nde Akulephelra Limodzi Ndi Boma Anthu Angophedwa Masana Ngati Tili Ku Somalia Kopanda Boma, Zala Ziwiri Nde Inapita Ndi Mwiniwake Anthu A Kumpoto Ali Pamphepo Nde Musalimbane Ndi MCP Ngati Mwadya Ma Bans Kt Muzsokoneza Musanza,… Read more »

TSAMBALIKAGWA
8 years ago

Sosten Gwengwe, George Zulu ndi Abel Kayembe ndi ana osakhwima Pamchombo awa, Ana opulukira, Mumati mutani inu? Mukanyoze Rt Hon JZU Tembo? Lero mukudzafuna chiani ku MCP, Mwana onyoza Makolo ake afe ndithu, Mukamfuse Lilian Kapanda, Kennedy Kalolo ndi Marget Maimba tinawaviinira Kazukuta ku Kasungu ndiku Dedza, These three Idiots must apologise to all the remarks they made against MCP and to Hon JZU in particular others no space for them in MCP, Anybody will be free to challenge Hon Chakwera at the Convention, MCP its a democratic party, Let’s work together for our beloved party MCP.

Achimidzimidzi
Achimidzimidzi
8 years ago

Mr Gustav Kaliwo has given a very intelligent answers. He is really mature.

So let democracy shake the weak out of leadership position. Even in the NEC, MCP should not behave like UDF or DPP kumasunga njoka.

Actually this is the right time for these infightings before general elections.

Stupid
Stupid
8 years ago

You can’t Njovu little boy, that’s rubbish . Njovu is more senior than chakwela even in terms of govt policies . Kodi anthu inu mwatani ? Aliyese wakale mchipanimu akhale mdani wanu? Rubbish ! Chakwela nesa ndiwe m’busa kodi ? Why are u failing to promote Love ? Mia come and take the party from these idiots .

mmm
mmm
8 years ago

Let Bisnowaty lead MCP. We need a complete change in Malawi.
Mzungu nthawi zonse amafuna kukhala pabwino.
Akalamulira Bisnowaty, Malawi izakhala wamkaka ndi uchi.

William Mzunga
William Mzunga
8 years ago

Abel Kayembe can only primary election only but not general election cos people of Dowa west were fooled they cannot repeat the same mistake MCP be careful u may lose seats to other parties

Read previous post:
Australia star renames Malawi Queens to Ma-WOW-ee!

Australia netball team goal defender  Sharni Layton praised Malawi Queens for their electric perfomance against New Zealand that fell just...

Close