Email a copy of 'Malawi court frees man who slashed fingers of boyfriend to ex-wife' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

95 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mavuto Pwiya~pwiya
Mavuto Pwiya~pwiya
8 years ago

Zoona, Anyamata alero amafuna kunyenga azikazi aweni kusokoneza mabanja aweni pamenepo anagamula muchilungamo ndizovuta zedi kupeza mkazi wako ali ndi wina mutu biiii! Umuluphira zedi. Anyamata Inu funsilani mkazi yemwe alibe mamuna, azimai ndi ambiri alibe azimuna.

Tengupenya
Tengupenya
8 years ago

Was the claimed divorce not proven???? If not, was the grievous bodily harm warranted by the chatting with the lady?? The victim should appeal. The court was being moralist here…

RoyK
RoyK
8 years ago

good judgement indeed. dont go for other pipo’s spouses; married or separated, uzafera gunkha.

kodulidwa zalako kakuoneka ngati kokwatila kale ndiyenso kamazembera mkazi wakenso

daneck Masoka
daneck Masoka
8 years ago

Yes of course the victim was wrong having an affair with undivorsed woman,the husband still deserve alittle punishment for putting the victimized disability which wil affect his day to day lifetime until death. Why did the judge skip this?

Mswazi
Mswazi
8 years ago

Muzikhapidwa choncho inu onyenga akazi aweni mxiiii. U make the husband lose temper, katundu ameneuja siogawana mwachisawawa muferapo. Zala zitatu zokha? Amayenela kuphedwa kumene!

del horno
8 years ago

poor judgement indeed…oweruza akutiphuzitsa ndikutilimbikitsa kuphwanya malamulo…no matter the circumstance but the chopper was supposed to punished backed by the law. ..anthu azingophana basi oweruza azingoti amayenda ndi mkazi wamwini uyu zake

xyz
xyz
8 years ago

Akadamupha, could he receive the same judgement?

Jijo
Jijo
8 years ago

ku Malawi Always ziphuphu basi.

Chambang'ondo
Chambang'ondo
8 years ago

Your worship Boaz. I salute you sir. This is the very best of judgments I ever heard. The procedure should be followed. Banja limathela ku khothi other wise she was still married. A Malawi chonde si onse olakwitsa amene ndiwolakwa. Bravo bwana Maxwell Boaz!!!

The "me"
8 years ago

This story is parading my whole inteligency,
1, kutha kwabanja amakuvomereza kukhothi basi kapena mboni zitatu achibale kapena ankhoswe ose ochokera mbali zose.

2, pa nkhaniyi padalibe umboni womveka bwino wosonyezadi kuti banja idatha,

3, judge sadalikwise amalawi tiphunzire kusata ndikuwaziwa malamulo a mmene tingakhalire

4, conclusion, mkaziyo panopa asankha ndani woduka zalayo kapena wankhanzayo?

Read previous post:
Blacks to release ‘Kuimba 10′ in July

After a long wait, Malawi’s leading  gospel outfit the Black Missionaries have finally announced that the much awaiting Kuimba 10...

Close