Email a copy of 'Malawi CSOs petition Mutharika, give 100 days ultimatum: Rains disrupt street protests elsewhere' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

96 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
JB
JB
9 years ago

Kodi ngoma ndi kabwira munali kuti pomwe Joyce Banda anatenga 73MMK ku NAC. Mitu yanu mwanva ndi MCP yanuyo

Andrew
Andrew
9 years ago

I dont want Muharikas. Why voting for dogs? He married when he became the stupid president, not married for years, stupid dog Mutharika. Chakuba mulungu akuwona naweso ufa ngati mkulu wako

superior singing method review

This can be interesting, since the reason that
body’s up there singing is usually to be noticed and
appreciated by others. Maybe you have tried to sing
a higher note as well as your voice actually starts to sound strained?
In Superior singing method sing you will find plyometric vocal exercises that will
help you enhance your vocal range. Usually it is simply an improvement inside the vowel.

aurora
aurora
9 years ago

these people have absolutely nothing to do…viva APM!! if you are tired go SLEEP

Anonymous
Anonymous
9 years ago

AMP is agood president l like his silence

lindiwe
lindiwe
9 years ago

Olo kukanakhala kopanda mvula anthu ake akanakhala omwewo. Maleaders a ma CSO 3/4 ndi akumpoto. Mulungubsazakupatsani mpata wolamulira mukapitiliza chonchi kuzikonda. Kuli Water for people anthu ogwira ntchito alipo 16 . 12 ndi a ku mpoto. Tiyeni yikondane a malawi. Tisalozane zala.panopa ana athu akukwatirana posaona ma regional boarders or tribes. We are all one . There is no elite group

Kanyimbi
Kanyimbi
9 years ago

Komanso izi ndiye zosekesa anthu 20 akuti akukatula madandaulo a anthu 15,000,000. Kuchita kuwonekeratu kuti alipo anawatuma. Ameneyo wangobetsa ndalama zache.

nyapala
nyapala
9 years ago

u so called xhigawenga! !! Ndwe Mbuxi ya Munthu(person_

Kes munthali
Kes munthali
9 years ago

Za ziii ! The only CSO I know is CAMA under Kapito, Ntambo, sembereka, Dorothy ng’oma, kwataine, Jessie Kabwila and Trapance are an alliance of opportunists, money hungry thieves and political failures worse than cockroaches. The reason people did not turn up is because, they are tied of being used as pawns in this dirty game, mwangwanayo anyani inu.

Mdicai Longwe
Mdicai Longwe
9 years ago

Inu a John Manyamba mademo onsewa akuchitikira ku mpoto kokha? Uku ndiye kulasa pambali kwenikweni. Nkhani ndi ya dziko lonse inu mukanyoza anthu akumpoto. Parliament building ili kumpoto mukuneko? Nanga anthu onsewo anali kumeneko anali akumpoto okhaokha? Chitani nthumanzi bambo osamangonena ngati zoona zake simukuziwona.

Read previous post:
Malawi demo runs peacefully: CSO’s hail police

Malawi civil society groups anti-government demonstrations in the capital Lilongwe  proceeded peacefully on Tuesday. Spokesman of the protests Timothy Mtambo...

Close