Email a copy of 'Malawi CSO’s rebuke ‘govt propaganda’ against Jan 13 demo' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

95 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Connex Chilaka Ogalu
9 years ago

Ma demo alipo basi kaya ka radio kena kapange ma intimidations otani

kk
kk
9 years ago

Mtambo ask Mwasungula he failed to control chigulu cha anthu chomwe anapita nacho ku mseu. Mind you there is no peaceful demostration. You cannot say it will be peacefull as if you know the kind of people who will go to the street with you. Let me educate you, my young boy, akamati anthu akukayenda ku mseu ngati demo ya dziko lonse, kumatuluka anthu okumwa mowa, osuta chamba, now there is no way you can control munthu wa chamba because chamba its like a drug munthu akasuta mutu wake sumayenda bwino. Ndi aja amayamba kumphwanya magrocery anthu, kuswa magalimoto anthu… Read more »

kk
kk
9 years ago

Opepela ndi amene azapite ku mseuyo, chifukwa chipolopolo chikakutibula ndikufa, wafela zako. Kodi ndi atsogoleri angati adafa nawo pa 20 paja. Ngakhale Mwakasungula ndi Rafik olo kukandika ata. Anafa ndi anthu ogundika ngati iwe ndi ine. Mmmene ndinawonela ine nthawi imene ija aMtambo simungandiputsise olo pang’ono. Ndithu tikafele 5million ya ku NAC, kodi moyo umagula ndi 5million? Mukanatiudza mwina kuti tichite demostrate because of Cash gate, jetgate, kapena chimanga chinaola mma silos chija zinali zomveka, chifukwa cashgate anali ma Billion ambiri, ndege inali ya ma billion, chimanga cha ma billion. Koma zoona anthu akataye miyoyo chifukwa cha 5 million ndiye… Read more »

chindi
9 years ago

thats stupid coment

Blameless
Blameless
9 years ago

Friends, the strategy of blaming it all on Tumbuka people has outlived its purpose. Malawians now know better. It is just not working – what with the hundreds of thousands of our kin from south and centre who are peacefully working and doing businesses in the north. We may have to convince these people first that the northerners who are accommodating them are actually evil people.. Let us just re strategize

Tyi
Tyi
9 years ago

Kunena chilungamo JB ndi bulutu. Martha Kwataine, Sembereka mbuzi za anthu.zoona munthu wanzeru angamamvere Trapence bulutu wachabechabe anachosedwa ku MRA chifukwa cha umbanda. Martha nae ndi mphuno zakozo. Atumbuka anthu omvesa chisoni nanu ndi mabulutu

mwiithotho
mwiithotho
9 years ago

Taaoneni a Mtambo, better for you to demonstrate in support of your’favorite’ federalism

Connex Chilaka Ogalu
9 years ago

Go ahead all NGOs

Kakha Erutu
Kakha Erutu
9 years ago

Ma profile a anthu amene akupanga phokoso wa sakundidalitsa olo pang’ono. These are frustrated non entities who are bankrolled by satanic organizations. Ongofunika kuwapemphelela basi.

wanted
wanted
9 years ago

The wakwithu are behind this

Read previous post:
Bullets give coaches ‘treble’ target in 2015

Bullets FC  Excecutive Committee has set a target of winning three major competitions in the coming 2015-16 soccer season to...

Close