Email a copy of 'Malawi effects 5pc hike on fuel: To have knock-on effect for transport, food costs' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

17 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Duduzane
5 years ago

A pathfinder kaya mumati ndani ndi munthu osaganiza ndipo mutu siukugwira. Ku rsa akwezadi mafuta katatu within a shot period of time koma still ku malawi mafuta akudula heavy. 900 pamene south africa ndi R13 . Olo atakweza ka ten still mtengo wa mafuta ku malawi uzakhalabe pa mwamba. Komanso ku south africa njoka yopezera ndalama siyivuta ngati ku malawi. Anthu ambiri akugwira ntchito

pathfinder
pathfinder
5 years ago
Reply to  Duduzane

Iwe duduzane usaname apa, mafuta ku SA ali pa R17 pa litre, zachamba eti kuzolowela kukwera ma minbus

pathfinder
pathfinder
5 years ago
Reply to  Duduzane

Ndiye uyipange R17 times 52 even 55 malawi kwacha upeza kuti ndichimodzimodzi, ungandiuze chiyani mbutuma ngati iwe

Shitholes Diarrhoea Progressive Party

Alamu Pumani Mwakalamba mukutipheranji? Those who will benefit are CEOs Amasungula.

Vinco
Vinco
5 years ago

What kind of government do we have??? Boma losaganizira anthu ake ??? Aaaaaaaa this government needs to go sure on 21 May, 2019. Mmene aMalawi tikuzunzikiramu, ndiye wina kupanga chigañizo chokwezanso mafuta??? Akufuna titani anthufe????? Mafuta akakwera chonchi, everything goes up as well!!!! DPP, ulendo wako, wakwana sure!!! Mmalo momawanyengerera a Malawi, mukuwafinyanso!!!!!!!

pathfinder
pathfinder
5 years ago
Reply to  Vinco

A Vinco taziganizani inu, malawi ilibe zitsime zamafuta, imachita kuyitanisa, tsono ngati mafuta akudula mayiko omwe amawenga mafutawo kulibwanji malawi?

braveheart
5 years ago

From 1/10/18 fuel in SA has gone up with R1..the highest increase in over 10 years or so..

Maclon
Maclon
5 years ago

@ Pathfinder, whether in other countries fuel prices are increasing every two months or not but know that people here are feeling the bite of these inflations. Most of those affected are the employed and jobless masses.

When somebody complains, it does not mean that they are ignorant.

They might be more informed than yourself. They way you articulate issues it seems you are an overzealous party loyalist.

Make Malawi Great
Make Malawi Great
5 years ago

actually those subsided fuel prices are higher we are only sitting on a time boom!

Bystander
Bystander
5 years ago

Whether Malawi is doing well or not what I know is that prices of all commodities and services are going to rise. Meanwhile my income shrinks

pathfinder
pathfinder
5 years ago

Ndizosadabwitsa izi, chifukwa ngakhale mayiko ochita bwino ngati SA mafuta akumakwera every two months. So amene angapeza ponyozera boma ndi anthu omweomwewo otsutsa, mbutuma za anthu zosadziwa kuti mmayiko ena zinthu zikuyenda bwabji chifukwa cha umbuli.

HoRror
HoRror
5 years ago
Reply to  pathfinder

Mbutuma ndi iweyo. Look take out rural electrification levy from fuel. Reintroduce it when u start producing enough power again. This fuel hike will imporse extra burden to the arleady burdened pple
Even road levy I dont know where the money goes coz most roads are donor/ngongole funded.

Mulomwe
Mulomwe
5 years ago

The single digit inflation rate is all cooked up. It has not translated and affected REAL people’s lives. Malawians are worse off than when Muluzi was in power. Stop taking the Malawi people for mugs – 21 May, tsiku lachigamulo. Some docile so called Maliseche needs to get a big boot to the head.

Bibo
5 years ago

Hedee tiyeni nazo!!! Ena akuti secondary school fees yikhale yaulele bwantchi kuyika ndalama kumafuta kuti ife a Malawi tiva kukoma boma mayika mtima pazikha zake

Read previous post:
Nico counting the cost of devastating fire

Officials at insurance company, National Insurance Company (Nico) say they are counting the cost of the fire which gutted most...

Close