Email a copy of 'Malawi fans want RVG to pack up and go: It is hard to disagree' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

6 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Nzika
Nzika
5 years ago

a Malawi ambiri titha kumakamba chinthu chofanana komano nthawi zina tizitha kuilowa nkhani mkati, kusiyana mkuti tiziti yes kamba koti majority ikuti yes,mukuganiza kuti RVG yo mpira sakuudziwa vuto si courch ayi choyamba muyang’ane kuti kodi mpira wathu uli bwanji mwachidule tisayembekezere flames kuchita bwino ngati national league yathu siili bwino mukufuna player akaphunzitsidwe kuchinya pa national level control yokhayo ngati wamenya pakhoma olo mutaitanitsa Zidane sizingatheke vuto ma courch omwe ali ku ma club sadziwa ntchito sadziwa kusula ma player.izizi ndi okhawo ochepa amene amautsata mpira atha kuvomerezana nane

chipatso mbewe
chipatso mbewe
5 years ago

Mponda ndiye woipa kwambiri, inu munthu anakanika ku kocha Wizard FC, ndiye mukuyembekeza kuti angakwanitse National team? And RVG sasankha ma players ndi iyeyu, amasankha ndi Mponda yu, chifukwa amalandira ndalama from the players kuti awachite feature mu game muja, dont hate RVG, he is innocent, muzazindikira bwino patsogolo a Malawi. Chifukwa chiyani mumakonda kumuyankhulitsa Mponda and not RVG when it comes to a Coach ayankhule pa radio? Who is the head Coach here? Mponda or RVG? It doesnt matter kuti RVG satha chichewa, had it been kuti amamuyankhulitsa pafupi pafupi, akanaphunzira by this time, but mumamuika kumbuyo kwa Mponda… Read more »

YNCM
YNCM
5 years ago

Uyuyu akapitiliza anthu azawaziwa kunali Buckerd Ziese naye ankatero

timathamangisa olo ku stadium

Harrison Tembo
Harrison Tembo
5 years ago

RVG Must go!!!! I wonder how Nyamilandu braggs about this useless coach eeeh!! Mr. Nyamilandu told us in his manifesto to retain the FAM POresidency that “This is the time to Harvest”. Now where is the Harvest? The time he was recruiting this failure Coach RVG he promised us the RVG would take us to AFCON Finals. Where are we? This is the time I can ably say, MR. Nyamilandu and RVG are a combination of NYUSENSI. RVG Must pack and go on 31rst March 2019 while Mr. Nyamilandu Must pack and go in December 2019. we build the national… Read more »

POOR MAN FEEL IT
5 years ago

AZIPITA ONSE ATATU ZOONZ MPONDA KUMUPATSA TEAM YAIKULU ANGATANI KULEPHELA KUITAN MZAVA MUNTHU OTI FULL GAME TIME PA JOLOZA OUT ONSE

JOHN MENARD WA MULINGA
JOHN MENARD WA MULINGA
5 years ago

APITE AMENEYO WATIKWANATU…….

Read previous post:
Malawi hosts international conference on ending gender-based violence

Offline and online internet facilities have posed a new challenge to efforts to combat sexual and gender-based violence (SGBV) across...

Close