E-Mail 'Malawi govt asks relatives to pay for air tickets of 12 girls stranded in Kuwait' To A Friend

Email a copy of 'Malawi govt asks relatives to pay for air tickets of 12 girls stranded in Kuwait' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
  Subscribe  
newest oldest most voted
Notify of
rio lucien
Guest
rio lucien

Anawatumiza ndani? Boma silinadziwe? Pamakhala ma police crealance, ma medical reports. Zonse ndi za fake. I have the names of all signatories. If somebody is serious, call me on 0888177520. I have all evidences

eliamk
Guest
eliamk

Agalu amenewa achimine anapitako bwaa? Abwere mmene anapitila not tax payers money shit

tizaona
Guest

Koma nde zero!!!! I don’t have president jst imagine anthu omwewo anakuvotelani ingakhale ma vote munabanso God is watching a munthalika muzapita ngati Gadafi ,you think ndikhani yomwela madzi basi nkukonza athuwotu ananamizidwa the kind of jobs they applied I think if you don’t have a comment sweetie leave it blank????

Thubwelubwe
Guest
Thubwelubwe

Moya pangani release money mukawatenge mahule amenewa tizidzachinda tokha kuno chondeeeee!

mr madotiro
Guest
mr madotiro

koma kuba ndalama eti? Inu aboma mukulakwa ponena kuti anthu alipililidwe ndi abale awo . Kodi anthu anapita ndi ndalama zao? Osagwira anthu omwe anawapitisao kuti awalipilire bwanji?. Nanga azamuufulu a anthu aja alikuti? .akawatengetu anthuwa.

Kokota
Guest
Kokota

INE NDISAPOTA WA DPP KOMA BOMALI LAFIKA POKUTI LIKUKHALA NGATI AKUTSOGOLERA NDI MWANA WAKHANDA TANGOGANIZANI KU SOUTH AFRICA KUNACHITIKA DZIWAWA ANTHU ANAKATENGEDWA NDI BOMA MWINA NDALAMA ZITHA KUMAKWANA 200 MILLION KODI ANTHU 12 KWALIPIRIRA NDEGE INGAKWANE YONSEYO KU MPIRA IKU NDALAMA ZIKUNGOSAKAZIKA OSASIYA ZA MPIRA MUKATENGE ABALE ANTHU BWANJI KOMATU AMALAWI OSAMATENGERA KUNTOSO NGATI MALIRO ANJOKA POMPANO ADZAFUNIKA NDITHU AMASINTHATU POYERAYERA NDE APRESIDENT PETER MUTHALIKA NGATI ANTHU AKUKUNAMIZANI NDITHU AKUKUPUSITSANI ANTHU NDIWOKWIYA KWAMBIRI BOMA ZOONA LIKALEPHERE KUTENGA KAPENA NDITI KUPULUMUTSA NZIKA YAKE KUCHOKERA DZIKO LINA YOMWEYO IDZAKABWERA MUDZIDZAYIUZA KUTI MUTITERE IFE TIPANGA CHITUKUKO MITU YANU IKUGWIRA NTCHITO OK POTI 2019… Read more »

pido
Guest

The girls are not from Lomwe belt hence government cannot afford to pay air ticket for them

zachep
Guest
zachep

Gvt managed to rescue thousands of Malawians from South Africa during Xenophobia. can it really fail to bail out the 12 girls? or was the Xenophobic attach planned for between the two govts?. Those who went to south Africa were seeking green pastures so too our girls in Kuwait. There is no difference between the two. So gvt should provide air tickets otherwise its another gender imbalance.

Thyolo Thava
Guest
Thyolo Thava

DPP iyo munavota nokha.. …ndalama kuthela kupangila misonkhano zina kulipila ma cadets and anthu oti adzitukwa Bushiri

KUWAIT MAN
Guest
KUWAIT MAN

How much is one way ticket from Kuwait that the Government can not afford to pay? How much was a hired Bus from South? Lets be serious, Malawi citizens are stranded out side the country and we say its the responsibility of parents!!!! The Government needs to take responsibility at all cost.